Malawi uja lero.

Malawi uja lero. Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi uja lero., Marketing Agency, Hong Kong.

Had it been kuti ineyo I was this minister sikunali kuyenera kupangira this press briefing mu WAREHOUSE. Fertilizer anth...
30/11/2023

Had it been kuti ineyo I was this minister sikunali kuyenera kupangira this press briefing mu WAREHOUSE. Fertilizer anthu mumamiziku akumusowa inu mukungojambulisilapo.

Kunali kwabwino kamawaonesa anthu fertilizer ali ku malo ogulisila .

Koma vuto fertilizer uyu simunalipire uja mukuzichemelera naye kuti afika uja ndalama palibe zoti mukalipire.

Kodi muzingowanamiza amalawi mpaka liti?

Anduna inu yemwe anakulangizani iziyo dziwani anakudyesani galu.

03/10/2023

Imfa ya chigawenga mdziko muno zisatiiwalise kuti mafuta agalimoto dziko lino mulibe.

Azimai ambiri akuyamikira nsalu iyi kuti ndi java olimba kwambiri..!!!
03/10/2023

Azimai ambiri akuyamikira nsalu iyi kuti ndi java olimba kwambiri..!!!

Malawi uja lero, eti Kodi zankhani ya mkulu uyu mukumuona apayi itipati?Malawi....  Ine ndwiiiii..!!!
03/10/2023

Malawi uja lero, eti Kodi zankhani ya mkulu uyu mukumuona apayi itipati?

Malawi.... Ine ndwiiiii..!!!

If you know you know.Madolo aja alikut lero?
03/10/2023

If you know you know.

Madolo aja alikut lero?

Malawi uja lero wafika pokuti ngakhare chakwera sakuziwa kuti kodi atani.Amalawi tinayenera tivomereze kuti tinanyoza ko...
03/10/2023

Malawi uja lero wafika pokuti ngakhare chakwera sakuziwa kuti kodi atani.

Amalawi tinayenera tivomereze kuti tinanyoza komanso kuchitira chipongwe munthu osalakwa.

Lero ndi zimenezi.

Power is in our hands let's do something on 2025 Elections.

02/10/2023

Malawi uja lero Kodi ku kenani kuja tinafikako kapena tidakali munjira kapena galimoto yaphwa ma tayala?

Pano tizifuna maganizo anu komanso nkhani zosiyanasiyana zochitikanso madera osiyanasiyana.

Tizithandizanso anthu ovutika munjila zosiyanasiyana.

You are welcome.

Address

Hong Kong

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi uja lero. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share