Charliey Mlakatuli BLK Mw

Charliey Mlakatuli BLK Mw Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Charliey Mlakatuli BLK Mw, Marketing Agency, Meleka, T/A Nkaya, Balaka.

Mutatipatsa ntchito yanu tigwiranso ndithu
06/02/2024

Mutatipatsa ntchito yanu tigwiranso ndithu

26/09/2023

TIZISAMALA NDI MALOTO OMWE TIMALOTA

Maloto ali magulu angapo ndipo umayenela uzindikile kusiyana kwa maloto amene umalota

Maloto ena amabwela chifukwa cha kuchiganizila kwambili chinthu ndipo maloto awa amakhala opanda tsogolo lililonse

Kulota ukuthamangisidwa koma osagwidwa, ukuoloka pa mulantho wa ntengo umodzi, ukudupha zenje, kapena ukuuluka malele, Imakhala khondo yomwe ikuchitika pamoyo wanu kuchoka kumidima ndipo Yehova akuoneselani ndi kukuululilani kuti akukumenyelani nkhondo ngakhale mukugona,
ndipo chomwe chimafunika ndi kudzuka ndi kupemphera kumuthokoza AMBUYE

Kulota zithu zoopysa monga ukumenyedwa, kapena uli matope ukukanika kutulukamo, penaso kumalota ukubanika mwina kumafuna kuti udzuke koma kumakanika, kulota zinyama zoopysa kapena malilo

Okondedwa iyi ndi khondo yoopysa ndipo ukapasidwa mwayi ozuka yamika Kumwamba chifukwa ambiri omwe amafela kutulo amakhala wakumana ndi khondo ngati izi, Ndipo izi zimachitika kwambiri pamene wagona osapephera "Nkhaniyi ndiyoonadi ndithu"

Kulota ukupha somba, ukukumba m'tedza ochuluka kapena ukukolola mbewu zimaimilila tsogolo lowala ndipo ukapephera patalike pafupike umazafikila ku chipambano ndi kulandila zomwe ziri zako

Kulota malilo matenda kapena kutha kwa ntchito ndipo pamapeto pake ndikuchitikadi, maloto awa ndi a uneneli ndipo samantchedwaso maloto ayi koma maso phenya ndipo zindikila kuti mwa iwe muli m'zimu wa uneneli ndipo ukakhulupilika posala kudya ndikupemphera m'phaso iyi imazaonekela pa iwe

Chofunika kuchita👉pamene mwalota zithu izi pinda bondo pempherani kususana ndi ma plan asatana pa moyo wa muthu yemwe mwamulotayo ndipo kukacha kamuuzeni kuti azipemphera kwambiri chifukwa wazungulilidwa ndi nkhondo

Kulota ukugonedwa kapena kugonana ndi munthu,

Pansi pa nyanja pali azimayi ndi azimuna omwe amakugona kumaloto ndipo akamakugona iwe umamva bwino mpaka pena kufika poziipisila, amakuoneselani nkhope ya m'kazi kapena mamuna wabwino cholinga ukomedwe ndipo amatenga m'phamvu yako nkupita

23/09/2023

You know why relationships don't last nowadays? 🤷‍♂️

Because we pay more attention to our phones than to our partners! 🙄

Nobody fights for love nowadays, everyone finds it easier to replace... 🌪

In these times it's so hard to find a good woman or a good man, no one wants responsibility, everyone is just looking for a non-committing relationships and no one dreams of having a home! 🙌🏻

Value your wife, appreciate and respect your partner, don't lose her or put your home at risk looking for beauty in people who have more effect than love… 🫥

Woman, take care of your husband. 🦾

And your husband takes care of you… 🔄

REMEMBER what is old for you is new to others!

Please Like 👍 and Follow ➡

23/09/2023

HOW IT TURNS SOUR!!

Was a beautiful day, birds singing smoothly!! Having a breakfast was not enough but sharing sweet talks with the loved one just to set a good flash back when am out.

Hugging, Kissing 💋 were some of spices on top of farewell to my journey by the duty call. I started up the engine 🚒 Off to work.

A day well spent, having fun with my hubby through zoom chat 💬, WhatsApping just to keep Her close that she may not feel loneliness.

Can't even believe, But I hate 😡 who introduce auto complete setting in mobile phone as well as computers. She asked me about accommodation where I took time to rest.

If I had known I could choose to end the matter by fall a false sleep. I responded calmly by saying everything here Is so marvelous, I really enjoyed the place and I wish you could be ,

Honestly, I was trying to type . By the time I arrived home 🏠, No one was at home, how can handle this, My God!! Please when you're much excited make sure you're right on your finger tip.

Please 👍 and ➡

20/09/2023

NTCHITO YANGA

Ndine ndithu yemwe uja,
Ndikavala makaka anga Munjenjemera Uyo Anatsomphora kanthu kamwini Pakuona ine Adzigamula ekha.......Cheka cheka aliyatsa liwiro losacheuka nalo MMbuyo.Ndioneka ine olungama pakulanga Ena,Koma Ntchito yanga yi Mbamba Yanditengera komkuja mmunda wa Eden njoka ija nde ndiyo duty yotisakaniza yi.

>Chibwana cha Mapira choyanika Maso Pa mtunda tong'otong'o,Mbalame zikazonkha,Mkuo ngwa mwini munda......
Nkanapilirira bwanji Mchisanu chazilakolako chodza ndi Mdimachi.Mutachita Kundisiya Ndi uyo Ondisautsa Mmalingaliro Oumbidwa bwino Work-mate.....Haaa! apa nde Mwatsekera Khoswe mu Mtedza sure Maferano Nyani ndi nthambi.......

>Fulukutu-fulukutu,Papasu-papasu,mbwandi-mbwandi wandigwira,akuchita kupuma chimkweza uku akunjenjemera nchiyani aWork-mate,Mwina mmalungo akulu...... Pawiri wiri Ntani nawo a work-mate.

>A a a a....Mpaka zafika pochotsana lamba?Nanga nkuwa bwanji poti wachitetezo ndine ndemwe......Mmalabada ziii.....a a a a Ntchito yanga ine!!!!! Ndikanena bwanji Kwa Munanga poti Ntchito yi/
usiku tipitiriza kugwira......Ndikanena Kwa O.C? ikanditembenukilatu nkhaniyi paja amati chigololo ndi mwini Chani chani kwinako.....Mayo ntchito yanga yandivulalitsa..

>mwina mukanatisinthira Uniform kutipatsa Ma Ovololo yotchinga nkumapazi komweku Mwina Ma Key bwenzi tikumasiya Ku nyumba kuti Ntchito zathu za usikuzi tisamaseweretse Chiwalo cha Okondedwa athu chi.......Nanga ngati ndi kwaya uotcheyi sitonse Chipere basi......Mayo o o o.....Ndati ntchito yanga Ana anga ndawasiya Pa Mavutotu Ine....
Chinkondwa cha Kholowachi cha zulitsa Mbatata pansi mbamba.......
Edgar ndi Devis ndakhulupilira Ntchito zina nzopweteketsa ndaonera Ntchito yanga.....

By !!
Like 👍 and follow➡

Address

Meleka, T/A Nkaya
Balaka

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Charliey Mlakatuli BLK Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share