Miss E-88

Miss E-88 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Miss E-88, Blantyre.

17/12/2025
17/12/2025

Bambo wa zaka 55, a Timothy Nkhoma, yemwe anali dalayivala pa chipatala cha St Anne's Mission m'boma la Nkhotakota afa atadziponya mu mtsinje wa Kaombe.

Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Nkhotakota, a Chisomo Chuma, wati a Nkhoma anachoka pa nyumba yawo atasiya lamnya ya manja ndikuuza mkazi komanso ana kuti asalondole komwe apita.

"Malemuwa anasiya chiphaso chawo choyendetsera galimoto komanso masilipasi pa mlatho wa Kaombe zomwe zinapangitsa anthu komanso apolisi kusaka thupi lawo mu mtsinjewu dzulo, koma tikuchitabe kafukufuku ofuna kudziwa chomwe achitira izi", atero a Chuma.

Malipoti ena , akuonetsa kuti chipatalachi chinayimitsa pa ntchito malemuwa kutsatira kubedwa kwa katundu, apolisi atachita kafukufuku anapeza kuti malemuwa siwolakwa ndipo anauza achipatalachi kuti awabwezeletse pa ntchito koma izi sizinaphule kanthu.

17/12/2025

Big shout out to my newest top fans! Mada Fune, Inallsaints Kanyesi, Happy Kumwenda, Ma Ry, Alufeyo Shongah, Unique Gee Kaizo, Wiseman Mphande, Chitokoto OG Trapper, ジミン メアリー, Codwl T Kalua, ဗီူဗီူဗီူ ဗီူဗီူဗီူ, Saw Call Cool, Jacob Hintarh Msango, ɭɭ J MAN ɭɭ, Tonga King, Noel Jonathan, Amos Skid, Spay Cgar Officer, Nah Brie Keneth, Careem Pekwe, Trick P Trick, Lennox Tantine, Victor En Drew Mboma, Throlacy Mphamba, ɭɭ Alex Chaona ɭɭ, Landlørd Gødfrêy Mw, Chinsinsi Sauka, Andrew Jere, Don Brandon, Francis Louis, Je Man, Okenzo MW, Chiku K Kasangula, Safiah Kalip

16/12/2025

Bwalo la Milandu kulilongwe lalesa a police amene anatenga Chilolezo kuti apite Ku farm ya Hon Simplex Chithyola kumene akuganizila kuti Kuli ma tumba a Boma a Feteleza ambiri.

Koma Bwalo laletsa aPolice kupitako kukapanga chipikisheni lawyer wao amene Alinso Lawyer wa Chipani cha MCP a Kazipatike atatenga chiletso.

Zatelemu a police alibe mphamvu yolondoloza matumba a Fetelezawa amene akuganizila.

Lawyer wa a Chithyola anauza Bwalo kuti a Boma sananene Ma Batch number a feteleza akukafufuza kotero asapite ndipo bwalo lamilandu linakhutila ndi mfundoyi ndikupeleka chiletso

Apolisi m’boma la Kasungu achenjeza anthu kuti asiye kufalitsa nkhani za bodza kapena zomwe alibe nazo umboni. Malingana...
15/12/2025

Apolisi m’boma la Kasungu achenjeza anthu kuti asiye kufalitsa nkhani za bodza kapena zomwe alibe nazo umboni.

Malingana ndi wofalitsa nkhani za polisiyi a Joseph Kachikho, mmawa uno a Runa James anapeza ng’ombe 8 zomwe zimangoyendayenda pafupi ndi nyumba za polisi za tsopano. A James ati anauza a police kuti ng’ombezo zikuoneka kuti zabedwa kwina kwake ndipo zinayi mwa ng’ombezo ndi anthu amene angosanduka mmatsenga.

Koma kafukufuku wa polisi anapeza kuti ng’ombezo ndi za mkulu wina wochita malonda a Yakubu Maleki zomwe usiku zinatchola khola kukasaka zakudya. Ndipo iwowo anakwanitsa kupezako ng’ombe 82 mwa ng’ombe 90 zomwe ali nazo.

Bail Granted for Mumba and Jessie. Senior Resident Magistrate Bracious Kondowe has granted bail to Malawi Congress Party...
15/12/2025

Bail Granted for Mumba and Jessie.

Senior Resident Magistrate Bracious Kondowe has granted bail to Malawi Congress Party member Vitumbiko Mumba and Malawi Congress Party spokesperson Jessie Kabwila who are answering a charge of Publication of false news likely to cause alarm to the public

Kondowe has granted the suspects bail on condition that they each pay bail bond of K1 million cash, produce one surety bonded at K2.5million non cash and surrender travel documents.

The two are alleged to have published a false statement titled We Got This which referred to an alleged electoral fraud by Democratic Progressive Party and the statement was made before MEC declared results of September 16 elections.

Bwalo la Chief Resident Magistrate Austin Banda ku Lilongwe lagamula kuti mlembi wamkulu wa chipani cha MCP a Richard Ch...
15/12/2025

Bwalo la Chief Resident Magistrate Austin Banda ku Lilongwe lagamula kuti mlembi wamkulu wa chipani cha MCP a Richard Chimwendo Banda amutengere ku chipatala kukalandira thandizo la mankhwala asadamupititse ku ndende kukadikirira tsiku lomwe mlandu wawo udzapitirire ku bwalo lalikulu(high court).

Ambali ya boma motsogozedwa ndi a Prescott Mwayiulipo anauza bwaloli kuti a Chimwendo Banda ndi a Alfred Dallah Kadula akuwaganizira mlandu wofuna kupha a Frank Chawanda mchaka cha 2021.

Iwo anati ndi koyenera kuti awiriwa awapititse ku ndende kuti adzikadikira tsiku lomwe mlandu wawo udzayambe ku High court ko potengera kuti bwalo la Chief Resident Magistrate siriyenera kuyendetsa milandu yokhudza kupha munthu.

Koma ambali ya oimira oganiziridwa mlanduwu a George Kadzipatike a Khwima Mchizi komano a Silvester Ayuba James anati sikoyenera kusunga a Kadula kaamba koti bwalo lalikulu la milandu lidapereka chiletso choletsa apolisi kupitirriza kuwamanga.

Kumbali ina, ambali ya oganiziridwawa anauza bwaloli kuti liloleze a Chimwendo Banda kuti akapeze thandizo la mankhwala ku chipatala cha kumtima kwawo kaamba koti chiwamangire akhala asakupeza bwino.

Iwo anatsindika kuti akadzachira, bwalo lidzawatumize ku ndende pamene adzidzadikira kuti mlanduwu aupititse ku bwalo lalikulu (High court) kuti ukayambe.

Wogamula mlandu a Banda anati pamene a Chimwendo apite kaye ku chipatala asadapite ku ndende, sangayankhulepo zambiri za a Kadula.

Anyamata oitanila minibus ndi ma taxi ku Msungwi mu mzinda wa Lilongwe awowoza (booing and heckling) munthu amene anaval...
15/12/2025

Anyamata oitanila minibus ndi ma taxi ku Msungwi mu mzinda wa Lilongwe awowoza (booing and heckling) munthu amene anavala attire ya father Christmas komanso kunuthira fumbi ndikumuvulanso zomwe anavala zo ati chifukwa father Christmas samayenda wapansi.

Anyamata wa anapanga izi uku akumunena munthu yi kuti zimene akupanga zi ndikunyozetsa gule chifukwa kudabwe kulibe attire ya father Christmas.

Dera la Msungwi linapanga chidwi ndi izizi pomwe anthu ambiri anabwera kuzawonela mnyamata anavala za gather Christmas yi akumuvula. Anamusiya ndi jersey ya Manchester United komanso boxer wa orange yemwe anavala mkati ndikumuiza azipita.

Breaking News...Police have apprehended Alfred Dala Kadula on charges of attempted murder, in connection with the same c...
15/12/2025

Breaking News...
Police have apprehended Alfred Dala Kadula on charges of attempted murder, in connection with the same case in which Richard Chimwendo, the MCP Secretary General, was also arrested.

Dala Kadula is currently being held at Area 3 Police Station.

POLICE LAUNCH MANHUNT OVER CHINTHECHE MURDER  IN NKHATA BAYPolice in Nkhata Bay have launched a manhunt for a suspect in...
15/12/2025

POLICE LAUNCH MANHUNT OVER CHINTHECHE MURDER IN NKHATA BAY

Police in Nkhata Bay have launched a manhunt for a suspect in the murder of Enwell Kayuni, 43, who was killed on Sunday night at Chintheche in the district.

Speaking in an interview Monday, Deputy Public Relations Officer for Nkhata Bay Police Station, Devoter Mithi, said the incident occurred after Kayuni invited Kettiness Sikwese, with whom he was in a relationship, to his house, despite the woman being separated from her former husband.

“During the night, Sikwese’s former husband forcibly entered the house while armed with a knife and started stabbing both Kayuni and the woman,” said Mithi.

Kayuni was pronounced dead upon arrival at Nkhata Bay District Hospital, while Sikwese was admitted to the same facility where she is currently receiving medical treatment.

Mithi added that the suspect remains at large and police have intensified investigations to apprehend him.

Kayuni hailed from Chautela Village, Traditional Authority Wasambo, in Karonga District.

Akuluakulu a chipani cha Malawi Congress (MCP) m'mawa uno akuchititsa msonkhano wa atolankhani kulikulu la chipanichi ku...
15/12/2025

Akuluakulu a chipani cha Malawi Congress (MCP) m'mawa uno akuchititsa msonkhano wa atolankhani kulikulu la chipanichi ku Lilongwe.

Mkulu oona zokopa anthu m'chipanichi, a Moses Kunkuyu, msungichuma a John Paul, mtsogoleri wa amai, a Jean Sendeza, ndi ena mwa akuluakulu omwe alipo pa msonkhanowu.

Padakali pano, a Kunkuyu akuwerenga kalata, mwa zina akudzudzula kumangidwa kwa mamembala a chipanichi, ponena kuti izi zikuchitika pa zifukwa zandale.

Lachisanu, apolisi amanga mlembi wamkulu wa MCP, a Richard Chimwendo Banda, komanso yemwe anaima ndi mtsogoleri wa chipanichi pachisankho chapa 16 September, a Vitumbiko Mumba, dzulo mneneri wa MCP, a Jessie Kabwira adzipereka okha ku polisi.

Chipani cha Umodzi chapereka masiku asanu ku boma kuti lifotokozere aMalawi pa zomwe lichite pa nkhani yofufuzanso za ng...
15/12/2025

Chipani cha Umodzi chapereka masiku asanu ku boma kuti lifotokozere aMalawi pa zomwe lichite pa nkhani yofufuzanso za ngozi ya ndege yomwe inachitika pa 10 June 2024.

Mtsogoleri wa chipanichi, Thomas Kaumba wanena izi pa msonkhano wa olemba nkhani mu mzinda wa Blantyre.

Izi zadza pamene mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika akuyembekezeka kufotokozera aMalawi ngati patachitike kafukufuku wina wa ngoziyi atalandira malipoti atatu kuchokera ku unduna oona za malamulo.

Kaumba wati zidziwika ngati boma la DPP lipange zosangalatsa aMalawi pa nkhaniyi kapena kuti linalonjeza za kafukufukuyi ngati njira yokopera anthu kuti awavotere chabe.

Address

Blantyre

Telephone

+265886909836

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Miss E-88 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Miss E-88:

Share