21/09/2026
Za English tikambabe koma nkhani ili pano ndiyakuti,
"Kodi mwakozeka kuteteza zomwe mwagwilira ntchito nthawi yaitali?.🥱 CIC Insurance Mw Life/General imapereka ma insurance solutions osiyanasiyana, kuphatikizapo Motor, Health, Life, Property ndi Business Insurance.
Musadikire mpaka ngozi kapena vuto litachitika. Funsani za insurance yomwe ikugwirizana ndi zosowa zanu ndipo tetezani zomwe zili zofunika kwa inu.
Mukafuna kudziwa zambiri apezeni on their page, you will be assisted