Lucius kulinji

Lucius kulinji Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lucius kulinji, Marketing Agency, Dedza.

Kodi yanu mwagula kale pezani yotsika mtengo lero
28/12/2023

Kodi yanu mwagula kale pezani yotsika mtengo lero

Khaaaaa
28/12/2023

Khaaaaa

22/12/2023

Pa samba ya nchezo ya whatsapp pakudutsa ichi nanu a seveth day mavomeraso kodi?,ndeno tithawire k*t abale😭😭

22/12/2023

Ku tiyeni kwapa Christmas box 🎁 ndi ukuku ma

22/12/2023

Mwadzuka bwanj nonse

Maule tsopano pamene tikumaliza chake akozeka Sunday lino
21/12/2023

Maule tsopano pamene tikumaliza chake akozeka Sunday lino

Yakwanuko mega farm dzina lake ndi chiyani
21/12/2023

Yakwanuko mega farm dzina lake ndi chiyani

Momwe timalizile Airtel top 8 chake Chino koms chomwe tikulowachi
21/12/2023

Momwe timalizile Airtel top 8 chake Chino koms chomwe tikulowachi

21/12/2023

So far momwe noma yachitila

Fdh : zero
Airtel: zero
Tnm: zero
Castle: pending

Chingamulo tamvomeleza koms tikukufunilan Christmas yopampana

21/12/2023


AMALAWI 1.5 MILLION ALI NDIMWAI OGULA ZIPANGIZO ZAULIMI ZOTSIKA MTENGO.

Nduna yoona zaulimi dziko muno a Sam Kawale ati mavuto omwe analipo pantchito yopereka zipangizo zotsika mtengo kwa alimi athana nawo.

Iwo ati amalawi okwana 1.5 million akuyeneka kupindula ndizipangizozi ndipo ati pakanali pano anthu omwe agula feterezayu akukwana 77 mwa 100 ali onse omwe akuyenera kugula.

"Pakanali pano unduna wazaulimi walipira kale ndalama zokwana ma tani 25,000 kukampani zogulitsa felereza ndipo uwonetsetsa k*ti aliyense oyenera kulandira alandire," anatero a Kawale.

Ndunayi yalimbikitsa amalawi k*ti asamangodalira ulimi wamvula koma adzipanganso ulimi wamthilira ndicholinga choti dziko lino lifzikhala ndichakudya chokwanira.

A Kawale alimbikitsanso amalawi kulima mbeu zina osati chimanga chokha kamba koti mvula yachaka chino ikhala yochepa.

Iwo ayankhula izi paulendo omwe akuyendera ma scheme atatu omwe akumangidwa m'boma la Nkhatabay.

21/12/2023

The Airtel Top 8 Cup final season Six is expected to be played in the first week of January, 2024, Football Association of Malawi reveals.

The development comes in after the FAM Appeals Committee's determination which ruled that Mighty Mukuru Wanderers have been booted out of the tournament after losing to Silver Strikers in the quarter-finals of the tournament.

In a notice released by the Association, Silver Strikers will face Mafco FC in the semi-final of the tournament on December 26, 2023 at the Bingu National Stadium.

"Appeal [of Mighty Mukuru Wanderers] is partly allowed in respect of the two sanctions of MK2, 000, 000 ( Two Million Kwacha) and MK500, 000. 00 ( Five hundred thousand Kwacha) for bringing the game into disrepute and failure to control fans which have been scrapped off.

"The rest of the Appeal is dismissed. The rest of the decision of the FAM Disciplinary Committee is upheld. ( Forfeiture of the match and the restitutory fine of MK22, 083, 400)," reads the press release in part.

FAM has scheduled the finals of the tournament for January 6, 2024 at Bingu National Stadium.

FCB Nyasa Big Bullets have already reached the final stage of the competition after booting out Civil Service United and Blue Eagles in the quarter-finals and semi-finals respectively, there y becoming the first team to reach the pinnacle of the tournament three times in three consecutive years, and they have a record of four tournament's finals.

Silver Strikers are the tournament's record winners after winning it twice while Bullets have lost two finals of the trophy in 2018 and 2022 to Blue Eagles and Mighty Mukuru Wanderers respectively.

21/12/2023

Address

Dedza

Telephone

+265990424480

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lucius kulinji posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share