26/08/2026
Katswiri wakuno ku Africa Sadio Mane wapulumutsa timu ya AI Nassr usiku wa la chiwiri.
Goalkeeper wawo anapatsidwa khadi lofiira pa mphindi 12, Al Nassr inagoletsedwa zigoli ziwiri mu gawo loyamba ndipo Cristiano Ronaldo adatulutsidwa gawo loyamba la masewero litangotha.
Koma chozizwitsa chinachitika mu mphindi 20 zomaliza ndi ma assist awiri ochokera kwa Joao Felix ndi zigoli ziwiri zochokela kwa Sadio Mane.
Timu ya Ange Postecoglou yagonja 3-2 ngakhale kuti inayamba ndikutsogola.