MBriefs

MBriefs ๐–ธ๐—ˆ๐—Ž๐—‹ ๐—‰๐—‹๐–พ๐—†๐—‚๐–พ๐—‹ multimedia source for bite-sized briefs ๐–ฟ๐—‹๐—ˆ๐—† ๐–ฌ๐–บ๐—…๐–บ๐—๐—‚ ๐–บ๐—‡๐–ฝ ๐–ป๐–พ๐—’๐—ˆ๐—‡๐–ฝ. Look no further, join the network, follow MBriefs - Zochitika Zakwathu!

Collins Magalasi amene adakhalapo mkulu wa nthambi ya BOMA ya MERA zaka zapitazo tsopano amupititsa ku ndende yaikulu ya...
03/09/2026

Collins Magalasi amene adakhalapo mkulu wa nthambi ya BOMA ya MERA zaka zapitazo tsopano amupititsa ku ndende yaikulu ya Maula komwe akakhale akudikira kwa sabata ziwiri asanamve pempho lake la belo.

Senior Resident Magistrate Shukrani Kumbani ndi yemwe walamula izi lero mbali ya boma itapempha kuti mkuluyu apititsidwe ku remand pamene akuyankha mulandu wozembetsa ndalama, komanso kuba ndalama pafupifupi 3 Billion Kwacha za Public Service Pension Trust Fund pogula Amaryllis Hotel.

MG2 Vice President Dr Jane Mayemu Ansah has met Miss International Africa Yollanda Chimbarami and Miss Universe Zimbabwe...
02/09/2026

MG2 Vice President Dr Jane Mayemu Ansah has met Miss International Africa Yollanda Chimbarami and Miss Universe Zimbabwe 2025 Lyshanda Moyas in Blantyre.

MBriefs National Update

McDonald Mtetemera has been appointed Mighty Wanderers head coach effective immediately.
01/09/2026

McDonald Mtetemera has been appointed Mighty Wanderers head coach effective immediately.

Hon Sameer Suleman will hold a press briefing on the formation of Joint Committee of Parliament on Wednesday 2nd Septemb...
01/09/2026

Hon Sameer Suleman will hold a press briefing on the formation of Joint Committee of Parliament on Wednesday 2nd September, 2026 at 11:30 AM

MBriefs National Updates

๐™๐š๐ค๐š ๐Ÿ๐ŸŽ ๐œ๐ก๐ข๐Ÿ๐ฎ๐ค๐ฐ๐š ๐œ๐ก๐จ๐ ๐จ๐ง๐š ๐ง๐๐ข ๐ฆ๐ญ๐ฌ๐ข๐ค๐š๐ง๐š ๐ฐ๐š ๐ณ๐š๐ค๐š ๐Ÿ๐Ÿ“Diof Simaone yemwe anali msilikali wankhondo ku Kamuzu Baracks amugamula...
01/09/2026

๐™๐š๐ค๐š ๐Ÿ๐ŸŽ ๐œ๐ก๐ข๐Ÿ๐ฎ๐ค๐ฐ๐š ๐œ๐ก๐จ๐ ๐จ๐ง๐š ๐ง๐๐ข ๐ฆ๐ญ๐ฌ๐ข๐ค๐š๐ง๐š ๐ฐ๐š ๐ณ๐š๐ค๐š ๐Ÿ๐Ÿ“

Diof Simaone yemwe anali msilikali wankhondo ku Kamuzu Baracks amugamula kukakhala kundende ndikugwira ntchito yakalavula gaga kwa zaka 20 atapezeka wolakwa pa mlandu wogonana komanso kupereka mimba kwa mtsikana wa zaka 15.

MBriefs National Update

Update on the Mozambique- Malawi (MOMA) 400KV power  interconnector. MBriefs | National Update
31/08/2026

Update on the Mozambique- Malawi (MOMA) 400KV power interconnector.

MBriefs | National Update

Nduna yoona ubale wa dziko lino ndi maiko ena, olemekezeka George Chaponda wapepesa anthu a mdziko la Norway pa imfa ya ...
31/08/2026

Nduna yoona ubale wa dziko lino ndi maiko ena, olemekezeka George Chaponda wapepesa anthu a mdziko la Norway pa imfa ya mfumu Harald (yachisanu) yomwe yamwalira pa 28 August 2026.

Poyamikira ubale wabwino wa Norway ndi Malawi, Chaponda wati president Arthur Peter Mutharika ndiwokhudzika kwambiri ndi imfa ya Harald yemwe anali ndi zaka zakubadwa 89.

Poimilira president wa dziko linoyu komanso a Malawi onse, Chaponda wakalemba m'buku la mauthenga a chipepeso ku ofesi ya kazembe wa dziko la Norway mdziko muno.

MBriefs National Update

Mighty Wanderers yaimitsa coach wake Bob Mpingajira. Izi zikudza Wanderers itagonja kwa Ekhaya FC mu ndime yotairiza ya ...
30/08/2026

Mighty Wanderers yaimitsa coach wake Bob Mpingajira. Izi zikudza Wanderers itagonja kwa Ekhaya FC mu ndime yotairiza ya Airtel Top 8.

Ekhaya yatenga chikho Cha Airtel Malawi Top 8 itapambadza Wanderers ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi pa Bingu Stadium ku L...
30/08/2026

Ekhaya yatenga chikho Cha Airtel Malawi Top 8 itapambadza Wanderers ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi pa Bingu Stadium ku Lilongwe.

28/08/2026

Mu nyengo ya uncle Evance Meleka. Lekani kuipitsa anthu ena, kupambana kwa ena kusamakupweteni mtima- kumaliopa mawa.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MBriefs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MBriefs:

Shortcuts

Share