Sumu Vyatowa Enterprises

Sumu Vyatowa Enterprises Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Sumu Vyatowa Enterprises, Marketing Agency, Lilongwe.

A Tokyo8 franchisee in Malawi promoting Japanese-inspired bio-fertilizer solutions for food security, climate-resilient agriculture, and sustainable livelihoods.

27/04/2026

It’s Monday!
​The secret to a great harvest is planning for the future today. Switch to Tokyo8 Bio-fertilizer to transform your soil and boost your crop yields—ensuring a fertile legacy for the next generation.
Contact us now 0885097974 or 0999279239

Ngati musanamuyese, tamuyeseni lero ndipo simuzakhumudwa
25/04/2026

Ngati musanamuyese, tamuyeseni lero ndipo simuzakhumudwa

Nthawi yopha makwacha ija ndi ino! Pezani Tokyo8 Bio-fertilizer wanu lero. Tsatirani bwino ndondomeko zonse zakasungulid...
23/04/2026

Nthawi yopha makwacha ija ndi ino! Pezani Tokyo8 Bio-fertilizer wanu lero. Tsatirani bwino ndondomeko zonse zakasungulidwe ka fertilizer yu zomwe taika pa chithunzi chili pansichi.
Imbani foni pa nambala izi 0885097974 kapena 0999279239

Check out this bean field in Kamwendo, Mchinji where our customer is using Tokyo8 Bio-fertilizer for his irrigation farm...
23/04/2026

Check out this bean field in Kamwendo, Mchinji where our customer is using Tokyo8 Bio-fertilizer for his irrigation farming. At Sumu Vyatowa, we provide full support and guidance to ensure your crops thrive.

​Watch this space, we will post the 3-week progress soon! Act Fast: The irrigation season is in full swing—get your Tokyo8 today.

Contact us now 0885097974 or 0999279239

13/04/2026

New Week, New Growth!
From soil to success — Tokyo8 Bio-Fertilizer is transforming Ujere herb fields with bigger yields, healthier plants, and greener landscapes.
Proof that the right boost makes all the difference!

Ambiri mukugona hahahaha ena akuona ngati AI hahahahaha Tokyo8 bio fertilizer ameneyu anawadzidzimutsa a Ujere Herbs ku ...
11/04/2026

Ambiri mukugona hahahaha ena akuona ngati AI hahahahaha Tokyo8 bio fertilizer ameneyu anawadzidzimutsa a Ujere Herbs ku mbeu zawo za Chidede. Mmene mukuoneramo mbeu zawo zachita bwino chifukwa cha chiganizo chabwino chomwe iwo anapanga pogwilitsa ntchito Tokyo8 bio fertilizer pa ulimi wawo. Ka ndalama kochepa, koma zokolola phwamwamwa.

Pezani wanu lero Tokyo8 bio fertilizer 0885097974 or 0999279239

11/04/2026

Eeeeh Tokyo8 bio fertilizer sizingatheke kupindulitsa mlimi! Eeeeeeh ndi maloto achumba amenewo. Chabwino! Ife tacheza nawo a Ujere Herbs amene anagwilitsa ntchito Tokyo8 bio-fertilizer mmunda wawo wa Chidede okwana pafupifupi 7 acres ndipo akusimba lokoma. Koma tisanacheze nawo uoneni munda wa chidede mmene wasinthira kenako timva mmene amagwilitsira ntchito Tokyo8 bio-fertilizer mmunda mwawo.

Pezani wanu lero Tokyo8 bio fertilizer 0885097974 or 0999279239

Kod mukudziwa kuti mbewu zanu za masamba monga kabichi (cabbage) zimachita bwino kwambiri ngati mwagwilitsa ntchito Toky...
09/04/2026

Kod mukudziwa kuti mbewu zanu za masamba monga kabichi (cabbage) zimachita bwino kwambiri ngati mwagwilitsa ntchito Tokyo8 bio-fertilizer? Mlimi uyu anayamba kugwilitsa ntchito Tokyo8 bio-fertilizer pa ulimi wake wa kabichi ndipo ali ndi chiyembekezo kuti mbeu zake zikhala zochuluka.

Pezani wanu lero Tokyo8 bio fertilizer 0885097974 or 0999279239

29/03/2026

Sumu Vyatowa Enterprise is transforming rice farming with Tokyo8 bio-fertilizer—healthier soils, stronger crops, and abundant harvests that fuel dreams.

Get your Tokyo8 bio fertilizer now on 0885097974 or 0999279239

23/03/2026

Do you Know?
Freshness Starts Here!
At Sumu Vyatowa Enterprise, tomato farming thrives with the innovation of Tokyo8 bio-fertilizer—delivering richer soils, healthier plants, and harvests bursting with flavor. From farm to market, we grow quality you can trust.

Agulu!Mwamuona Tomato uyu, Tokyo8 bio fertilizer wagwira ntchito ngati mthandizi mnyumba mwanu. Chisankho chanu cha lero...
06/03/2026

Agulu!
Mwamuona Tomato uyu, Tokyo8 bio fertilizer wagwira ntchito ngati mthandizi mnyumba mwanu. Chisankho chanu cha lero chikhoza kusintha umoyo wanu ngati mwagwiritsa ntchito Tokyo8 bio fertilizer lero.

Contact us now on 0885097974 or 0999279239

Agulu, Tabwelani. Lero tingolitchula Natty Day. Nkulakwa kutelo?😃The mastermind behind Sumu Vyatowa Enterprise, Natty Mt...
05/03/2026

Agulu, Tabwelani.
Lero tingolitchula Natty Day. Nkulakwa kutelo?😃

The mastermind behind Sumu Vyatowa Enterprise, Natty Mtika, was born on this day some decades ago. Tiyeni tiwalembere mafuno abwino mu comment section ndipo ife tiwatumizira kuti mwina tsiku lina mkutidzidzimutsa ndi ka Tokyo8 Bio Fertilizer 😁.

Happy birthday Madam. 🎁🎉

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sumu Vyatowa Enterprises posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share