Mikoko

Mikoko Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mikoko, Advertising/Marketing, Mulanje.

19/12/2022

Kodi studio 25c ilipati

19/10/2022

06/09/2022

AMALAWI

Dziko lathu silikuenda bwino chifukwa chaife tomwe lets unite kupanga magulu kuti boma komaso amabungwe athe kutithandiza ngongole zamudzi.

panopa siakumudzi kokha omwe akuvuti komaso mtown momwemu achinyamata tikuvutika poyambila tilibe lets stund and fix malawi


NGONGOLW SIMAKHALA K300 TISATHAWILE KUNJA TIPHEDWA ZAZIIIII

06/09/2022

Lol.. Don't drained your power for phonograph.... Let's use the power to unite and dill with our country..... Kupita ku Joni sikuthesa upawi...

Hi Malawi....Tisakhale ngati tamuiwala Martse Foundation....Lelo tikukwanitsa miyezi iwili chichokeleni mwana wathu    m...
23/07/2022

Hi Malawi....

Tisakhale ngati tamuiwala Martse Foundation....

Lelo tikukwanitsa miyezi iwili chichokeleni mwana wathu ma dziko lino...

Apolice sakuonesa chidwi chilichonse pa khani ya imfa ya nyamata ameyu ndipo akubanja akuti mwana wao sanafe pangozi ai koma anachita kuphedwa... Ndi kabungwe kakumidima komwe kakhala kakumusaka martse..

Kutengela ndi mene wayakhulila mkulu wake wa matse wati iye sasiila panjila mpaka chilungamo chiende ngati madzi....

    walila mokweza kupepha athu kuti amuthandiza kupanga promote lunso lake kunena mosabisa nyamata amatha kuimba mwina ...
22/07/2022

walila mokweza kupepha athu kuti amuthandiza kupanga promote lunso lake kunena mosabisa nyamata amatha kuimba mwina mwamuiwala😜

ndi modzi mwa oimba omwe amaimba zomveka bwino zangovuta kuti athu samuthandiza mukudziwa inu music ndi ndalama ndi chiseko ndi felemu.....

ONE DAY MALAWI WILL SUPPORT YOU.

Hi anamkungwiI know AMBILI taimva khani ya mzimai mzathu  NYAU-YU.Akuti pali muthu yemwe amamukakamiza kuti agone nae nd...
11/07/2022

Hi anamkungwi

I know AMBILI taimva khani ya mzimai mzathu NYAU-YU.

Akuti pali muthu yemwe amamukakamiza kuti agone nae ndipo amuthandiza ndi 10Million zikatheka zogonanazo....

Koma iye anakanaka ndipo akufuna aitengele kubwalo lamilandu mkuluyu kuti alandile chindapusa inu mukutipo chani Anamkungwi!!

FUNSO kumati :

1.KODI ZOONA MUTHU ANAGATULUKILA NDI 10MIllin kumati bwela tinye bwide dzuwa lake ilili?

2. Ngati zili zoonadi mukuona kuti nyauyu angagwilitse nyila yanji kuti athane ndivutoli.....

See u on comments Box..

27/05/2022

Azibambo akati amasuke 😀😀

Rest in peace
23/05/2022

Rest in peace

Address

Mulanje

Telephone

+27681146435

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mikoko posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share