Zinazake Mesa

Zinazake Mesa Turning Vibes into Entertainment, Every Day. About music

22/08/2026

A Thonx kuionetsa Dance ku Balaka stadium 🔥🔥🔥🔥

Iyi Mupweteka gulu boiz🔥🔥🔥Iyi Admin avala nawo😁🔥🔥
22/08/2026

Iyi Mupweteka gulu boiz🔥🔥🔥Iyi Admin avala nawo😁🔥🔥

Afisi Aku Ntcheu wooooh mesa nde Ifeyo!!!Iyiso akuti Ku chingoniko mukaiona ndithu☺️🔥🇲🇼Awa ndi ma 30pin , pomwe a "Angon...
22/08/2026

Afisi Aku Ntcheu wooooh mesa nde Ifeyo!!!
Iyiso akuti Ku chingoniko mukaiona ndithu☺️🔥🇲🇼Awa ndi ma 30pin , pomwe a "Angoni Aku Ntcheu" ma 25pin...

For more information contact Travis Atsoh Mesa

Mupezetsen nyumba ya rent A round Ntcheu Boma… Ngat ilipo  Nenan ku comments box mulumikizane…
22/08/2026

Mupezetsen nyumba ya rent A round Ntcheu Boma… Ngat ilipo Nenan ku comments box mulumikizane…

22/08/2026

Ngati ku mtundu kwanu amadalira iweyo, Mulungu akukumbukile week ino! Amen

Some relationships just now!
22/08/2026

Some relationships just now!

The mausoleum for the late Legendary Sir Soldier Lucius Banda has been launched..Legacy still lives on🙏🏿🙏🏿 🕊️🕊️
21/08/2026

The mausoleum for the late Legendary Sir Soldier Lucius Banda has been launched..Legacy still lives on🙏🏿🙏🏿 🕊️🕊️

We are here with good news!! Ma t-shirt A "Angoni Aku Ntcheu" akutsikira mbali yakumeneko, kuyambira pa 25 August 2026 ,...
21/08/2026

We are here with good news!! Ma t-shirt A "Angoni Aku Ntcheu" akutsikira mbali yakumeneko, kuyambira pa 25 August 2026 ,akhala Ali mu Ntcheu mo !! Pa Mphate Boma , t-shirt iliyose ,colour iliyose,size Iliyose 25pin basi...Koma pa tsiku lachingoni azakhala ma 30pin only basi...nde zili ndi iwe!!! Serious customers place your orders!!! Abwere size yanji komaso ntundu wanji???☺️🇲🇼🔥

For more info contact Travis Atsoh Mesa

Happy birthday to our topfan, Frank chazala 🎁🎉🎊 Mupatsen mafuno Abwino…
21/08/2026

Happy birthday to our topfan, Frank chazala 🎁🎉🎊 Mupatsen mafuno Abwino…

AkufunA kwabwno amene mwatola katundu wamunthuyu muimbren manambala ake waika pompo muthandizen….🥲
20/08/2026

AkufunA kwabwno amene mwatola katundu wamunthuyu muimbren manambala ake waika pompo muthandizen….🥲

Address

Ntcheu

Telephone

+265998327355

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zinazake Mesa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share