NYAKA Private School

  • Home
  • NYAKA Private School

NYAKA Private School Your Child's future is our concern!

Tumizani mwana wanu ku NYAKA NURSERY AND PRIMARY SCHOOL and simudzakhumudwa chifukwa YOUR CHILD'S FUTURE IS OUR CONCERN.
16/08/2023

Tumizani mwana wanu ku NYAKA NURSERY AND PRIMARY SCHOOL and simudzakhumudwa chifukwa YOUR CHILD'S FUTURE IS OUR CONCERN.

In Collaboration with a friend pa Nsanje boma we have opened another school in the name Exodus Private Nursery School.At...
16/08/2023

In Collaboration with a friend pa Nsanje boma we have opened another school in the name Exodus Private Nursery School.
At this campus, we looking for dedicated and caring nursery school teachers.
The applicants must have MSCE and fluency in speaking of English.

We had wonderful moments yesterday on 19th November 2021.Congratulations to 21 students who have completed a preschool c...
20/11/2021

We had wonderful moments yesterday on 19th November 2021.
Congratulations to 21 students who have completed a preschool course at Nyaka Private School and they are starting std 1 in January.

NYAKA PRIVATE SCHOOLNURSERY SCHOOLMwana wanu adziwe kuwerenga ali ku Nursery.Kuwongola mtengo mpamene uli wawung'ono.Kho...
04/10/2020

NYAKA PRIVATE SCHOOL
NURSERY SCHOOL
Mwana wanu adziwe kuwerenga ali ku Nursery.
Kuwongola mtengo mpamene uli wawung'ono.
Kholo la nzeru limakonzeratu tsogolo la mwana.
Tsogolo la mwana wanu lili mmanja mwanu.
Tumizani mwana wanu lero.
Malo: kuseli kwa nsika wa pa Mbenje kwa Khomero.
Nthawi: 7:30 mammawa.
Fees: K2000 yokha basi pa mwezi.

PART TIME CLASSES
Mwana wanu wakhalitsa pakhomo chifukwa Cha COVID 19. Koma musadere nkhawa. Tirinso ndi maphunziro a ophunzira akuprimary. Mwana asasewere kuyiwala za ku sukulu.
Nthawi: masana ana anu akaweruka ku sukulu.
Fees: K1000 yokha basi pa mwezi.

Your child's future is our concern!!!!

24/12/2019

First term yatsekeredwa tsopano. Ndipo second term ikutsegulilidwa pa 6 January 2020. Chosangalatsa mchoti, ophunzira omwe adapanga graduate pa NYAKA PVT NURSERY SCHOOL 2019 ndikukhonza mayeso okayambira STD 1, akhonzanso bwino mma primary schools mwawo chifukwa amakayamba sukulu akutha kuwerenga kale Chichewa ndi mawu ena amu English. Pa Mchere primary school, pa number 1 mpaka 4 mu std 1, pa number 1 ndi 2 mu std 2 adali ophilunzira ochokera pa NYAKA PRIVATE SCHOOL. Malo adakalipo tumizani mwana wanu lero!

Call 0997621400/0881082212/ 0993923357.
Email: [email protected]

YOUR CHILD'S FUTURE IS OUR CONCERN!!!

Tsiku lotsekera mu July 2019!!! Ophunzira 6 passed with distinction.. there are able to read chichewa right away from Nu...
13/10/2019

Tsiku lotsekera mu July 2019!!! Ophunzira 6 passed with distinction.. there are able to read chichewa right away from Nursery school. Akayamba standard 1 pa Mchere FP school. Ena Ali ndi zaka 4 mwa Ana amenewa.. others with credits and others with passes!

Address

Mbenje Trading Center

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00

Telephone

+265997621400

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NYAKA Private School posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to NYAKA Private School:

  • Want your business to be the top-listed Advertising & Marketing Company?

Share