Abdul Rachid amidu

Abdul Rachid amidu contact me wsp 📞+27781615578 [email protected]

07/05/2026

Mamuna aliyense amafuna mkazi okongola
Funso mkazi okongola yo za deen ali nazo?
Osamangoti bola amakwanitsa kupika swalah saswali

07/05/2026

Asalam allaykum warahamtullah wabarakatuh

Or akhale biliyonera us ka ndani osewo Malo awa azagona. Chofunika munthu aliyense achimike kugwira ntchito yomutamanda Allah chifukwa manda muli zilango ku manda kulibe kupuma ngati mene amanenera anthu akuti akapume inu adakuwuzani dani kuti kumanda ndikupumilako?

Asalam allaykum warahamtullah wabarakatuhIlibe phindu phone siikugwiritsidwa nchito kufalitsa tawhid ndi Sunnah.Komanso ...
23/04/2026

Asalam allaykum warahamtullah wabarakatuh

Ilibe phindu phone siikugwiritsidwa nchito kufalitsa tawhid ndi Sunnah.

Komanso kuletsana zinthu zoipa kulamulira zabwino.

Abdul Rachid amidu
Abdul Rashid Amidu

15/04/2026

Kudana ndi Sunnah kumati sindisakwatira koma uku mukuyenda zosalongosoka.
Abdul Rachid amidu
Abdul Rashid Amidu
Khalani otsatira Sunnah ya mtumik Muhammad s.w.a

15/04/2026

Chislam ndi chipempezo cha Mulungu Qur'an 3 vs 19.
Chikhrisitu ndi vs lanji likupereka chilimbikizo kuti ndi chipempezo cha Mulungu?

13/04/2026

akut chifukwa Cha social media usamadzuzule ma sheikh 🤣🤣Oro sizikhala zolakwika
umbuli si chinthu.😫

13/04/2026

Abdul Rashid Amidu
Allihamdulillah for everything

09/04/2026

Amwene kutamangiza ma files ko ndi kumeneko. Koma don't forget 7 minutes for swalah.

07/04/2026

Litima jealous siyabwino ngati mzanu wapeza chinthu chabwino Inu mungoyamikira next inu so muzapeza🤝

Address

Lanesia
Johannesburg
[email protected]

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Abdul Rachid amidu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share