Cargo Owners Association Of Enukweni

  • Home
  • Cargo Owners Association Of Enukweni

Cargo Owners Association Of Enukweni It's all about business

MUKUDZEYI MAKOMBE (JAH PRAYZAH)Mukudzeyi makombe, mwana wa john ndi shirley, anabadwa pa 4 july 1987 ku nyadire mission ...
13/08/2025

MUKUDZEYI MAKOMBE (JAH PRAYZAH)
Mukudzeyi makombe, mwana wa john ndi shirley, anabadwa pa 4 july 1987 ku nyadire mission ku uzumba ku zimbabwe. Mu banja la ana 5 koma 2 anamwalira. Iye ndi omaliza m'banjamo.
Mu umwana wake. Iye amakonda kulemba ndi kuwerenga ma novel abambo ake. Omwe adali a teacher pa school ina komanso amakonda kusambira ndikusaka nyama(ulenje).
Mukudzeyi adaphunzira pa musamhi primary school ndi musamhi secondary school ku murehwa kenaka adapita ku harare kwa uncle ake komwe adakaphunzira pa sukulu ina.
Zoimba adaziyambira ku school ndipo ankaimba reggae ndi dancehall koma nyimbozi zimangotchuka mu ghetto momwe amakhala. Mukudzeyi adayamba kuimba afro jazz ndi dj thando ndipo adaimba nyimbo ngati "sorry mama". 2007, adatulutsa album yoyamba ya "sungano" kenaka ma album ena awiri. 2013, mukudzeyi adatulutsa album ya chi 4 ya "tsviringo", imene mudali nyimbo ya gotchi gotchi yomwe idakhala song of the year. Mukudzeyi anatchuka kwambiri ndi nyimbo ya "mudhara vachauya" komanso "watora mari". Mukudzeyi waimbapo ndi diamond, mafikizolo,Yemi Alade, oliver mtukudzi ndi davido.
Mukudzeyi amatchedwa JAH PRAYZAH kamba koti dzina lake limatathauza kuti BLESS JAH ndipo iye ankafuna kulowa usilikari koma kamba ka mayi ake, zinakanika ndipo kuyambira pompo, jah prayzah amavala ngati msirikari pamodzi ndi band yake ya 3rd generation. Iye adatenga chilolezo kuchokera ku zimbabwe defence force kuti azivala za usilikari poti ndi ambassador wao.
Jah prayzah adapezeka ndi mlandu wothawa a police ndi azamiseu ku shurungwi kamba koyendetsa galimoto yosalembetsa ya mercedenz benz e320 ndipo adamugwira ku gweru.
Jah prayzah adakwatira rufaro chiwureso, yemwe adabereka naye ana akazi atatu ndi wa mamuna m'modzi.
Mukudzeyi jnr
keana
keyla
kelly
Jah prayzah ndi oyimba oyamba ku zimbabwe kuwina mtv award.
Jah adagwitsa ntchito ndalama zokwana $7000 pa birth day ya mum ake ndipo adagulitsapo cd pa mtengo wa $12000 yomwe ndipafupi fupi k21million.
Kupatula k

MALI 🇲🇱: President ASSIMI GOÏTA revealed some secrets about FRANCE 🇫🇷 when he sacked them.Read this and you will underst...
06/05/2025

MALI 🇲🇱: President ASSIMI GOÏTA revealed some secrets about FRANCE 🇫🇷 when he sacked them.

Read this and you will understand how evil the French are.

He said that “when they asked the French to leave, they went to gather all the terrorists and armed groups in Anefis to fight against MALI 🇲🇱 based on tribalism and religion.

They reached out to General GAMOU, whom GOÏTA has now appointed governor of Kidal. General Gamou who by the way is a Tuareg, told them that he will never fight the army and people of his country. He only fights the enemies of his country. So, he refused.

Now, some selfish people left Gamou and followed the evil men to fight their country. Their goal was to create a division between “blacks” and “white” (Arabs, Tuareg) skinned people. The Toubabou (white). The French tried this in Anefis when they were leaving. Thank God, they didn’t succeed”.

“So, after that, they started spreading false information that Gao was going to fall, that it will be attacked, all this to make the people flee their homes. But, I would like to thank the people of Gao who stood by their army. They spread pamphlets saying that Gao would be attacked.

After that, they have two terrorist groups: the Islamic State and JNIM. What they were only fighting is ISIS, not JNIM. Their General at that time had a map of where the two terrorist organizations were operating.

So, I asked them, are both organizations not terrorists? They said, no, we only fight ISIS. And yet, both organizations are fighting against us. However, when they were leaving, they tried to use both terrorist organizations.

With the former President of NIGER 🇳🇪, MOHAMMED BAZOUM, they said that they must promote social cohesion. At the same time, UN_MINUSMA 🇺🇳 was also leaving our country.

They scared the people by spreading rumors that Menaka will fall, Menaka will fall. But the soldiers protected Menaka to prevent it from falling.

At the same time, MOHAMMED BAZOUM released all the leaders o

PALI TSOGOLO LOTI POMPANO AFRIKA LITHA  KUKHALA DZIKO LIMODZI CHIYAMBI:Tikamawelenga mbiri ya Africa, mu zaka za mma 194...
02/05/2025

PALI TSOGOLO LOTI POMPANO AFRIKA LITHA KUKHALA DZIKO LIMODZI

CHIYAMBI:
Tikamawelenga mbiri ya Africa, mu zaka za mma 1940-50 ndi pomwe njala yofuna kuzilamulira okha (anthu a chi Afrika) inayamba mkumanka nikula. Njala imeneyi inaonjezekera ndi chikhulupiliro chomwe chimatchedwa Pan-Africanism chomwe otsatila ake amakhulupilira kuti anthu a nkhungu lakuda ali nkochokera kapena muzu (root) yofanana kotero akuyenera kubwera pamodzi ndi kutsutsana ndi nkhaza zomwe atsamunda amachitila anthu a khungu lokuda.

Ambiri omwe ankatsogolera chikhulupiliro cha Pan-Africanism sanali anthu oti ali mu Africa muno. Ambiri anali anthu a khungu lokuda omwe amaphuzira mayiko aluya / azungu. Ndakatulo ya mkulu wina otchedwa AIME CESAIRE , yomwe mutu wake amati "RETURN TO MY NATIVE LAND" inatathauzilidwaso mogwilizana ndi chikhulupiliro chimenechi.

Manthero azonse tinaona mayiko ambiri a muno mu Africa akuzigulira ufulu ozilamulira. Ndipo zinatheka .

Koma mayiko aluya/azungu akhalabe ali ndi phanvu pa mayiko a mu Africa mu njira zambiri. Kutilamula zochita munjira zambiri, zomwe ena anatathauzira kuti ukapolo sunathebe ndipo chikhulupiliro cha Pan-Africanism chija chikuyemera kufalikila ponse ponse kufililira mayiko a mu Africa atabwera pamodzi mkumazilamulira mwa okha.

Mbuyo monsemu president wa mu Africa aliyese yemwe amayesera kuonetsa mawanga a chikhulupiliro chimenechi amaphedwa, mwachitsanzo Sankara, Gaddafi, ndi ena.

TSOGOLO:
Pano kwabweranso Mtsogoleri wina m'dziko la BokinaFaso yemwe akutchedwa Ibrahim Traole, iye akuoneka kuti ndi ozikoka mu chikhulupiliro chimenechi cha Pan-Africanism. Pa zaka zochepa zomwe wakhala President atalanda ulamulilo wasitha zambiri m'dziko lake ndipo wathesa ulamulilo wa ma French m'dzikomo.

Nayeso anapangilidwa upo oti aphedwe koma mwa nwayi za ululika. Izi zapangitsa kuti anthu ambiri a nkhungu lakuda ayambe kumutamanda. Masiku apitawo ngakhale anthu ena a khungu lakuda omwe ali mmaiko aluya/azungu anali pa ulendo wandawala kupele

24/04/2025

What could you do?😅

24/04/2025
24/04/2025

This will be the greatest movie ever

23/04/2025

Zinthu zake💔

Renowned actor Tumpe Mtaya, popularly known as Phwedo, will appear at the Lilongwe Magistrate Court tomorrow.Mtaya was a...
23/04/2025

Renowned actor Tumpe Mtaya, popularly known as Phwedo, will appear at the Lilongwe Magistrate Court tomorrow.

Mtaya was arrested on Tuesday for allegedly having sexual activity with a minor, pending medical examination on the victim.

Central West Region Police spokesperson Foster Benjamin said on Wednesday evening that Mtaya has been formally charged with having sexual in*******se with a child , in line with Section 138 of the Penal Code.

Benjamin says following the results of medical examination, Mtaya has been formally charged and that he will be taken to court on Tomorrow where he will take plea.

A growing wave of frustration among Burkina Faso’s diaspora erupted onto the streets of Paris this week, as hundreds of ...
23/04/2025

A growing wave of frustration among Burkina Faso’s diaspora erupted onto the streets of Paris this week, as hundreds of Burkinabe citizens gathered to call for the resignation of the country’s transitional military leader, Captain Ibrahim Traoré.
Read full story @ iloveafrica.com

23/04/2025

Revenge went wrong 😂

Greatest quote ever
23/04/2025

Greatest quote ever

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cargo Owners Association Of Enukweni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Advertising & Marketing Company?

Share