The New Flames

Itinéraire Site Web Contacter l'entreprise

The New Flames Genuine Page where latest News are found

FOOD FOR THOUGHT MCP now needs a leader who doesn’t run when things get tough — a real field commander. After those tear...
24/05/2026

FOOD FOR THOUGHT

MCP now needs a leader who doesn’t run when things get tough — a real field commander.

After those teargas scenes, people are rethinking everything.

Members want someone bold enough to catch a teargas canister with bare hands, throw it back, dust off the smoke, and continue leading the struggle without hiding behind press statements.

24/05/2026

KABWILA WACHEZETSA ANTHU AKWA NSUNDWE NDI MAWU ACHILIMBIKITSO

Mneneri wachipani cha Malawi Congress Party(MCP) Hon.Prof. Jessie Kabwila,lero Lamulungu anakacheza ndi anthu akwa Nsundwe kuli Lilongwe pofuna kuwalimbikitsa kuti asataye mtima kapena kuda nkhawa ndi nkhanza za boma la DPP zomwe anawachitira sabata latha.

Poyankhula pa mwambo wochezera anthuwa Kabwila wati boma la DPP labalalika ndikulephera kwawo kuyendetsa dziko lino m'malo mwake achita chiwewe pongofuna kuzunza aliyese wotsatira chipani cha MCP popanda zifukwa zenizeni kotero walimbikitsa anthuwa kuti akhale olimba pa chipani chawo cha MCP asagwedezeke.

Sabata latha anthu pafupifupi khumi ndi m'modzi anamangidwa kumadera a Nsundwe,Mbwatalika,Mpingu ndi asilikali ankhondo komaso apolisi omwe anakachita chipikisheni usiku kumaderawa atanamizidwa kuti anthu kuderali akusunga zida zoopsa kuphatikizapo mfuti zomwe analephera kupezako ingakhale imodzi.

M'modzi mwa anyamata wakuderi wati Mzachidziwikire kuti a police sanapange zinthu zija mkufuna kwawo koma kulamulidwa ndi anthu a Ndale zomwe Iwo akuti sizinawanjenjemeletse olo mpang'ono pomwe.

JESSIE THE FEARLESS GENERAL.

Adresse

Victoria Avenue, Blantyre
Democratic Republic Of The

Notifications

Soyez le premier à savoir et laissez-nous vous envoyer un courriel lorsque The New Flames publie des nouvelles et des promotions. Votre adresse e-mail ne sera pas utilisée à d'autres fins, et vous pouvez vous désabonner à tout moment.

Contacter L'entreprise

Envoyer un message à The New Flames:

Raccourcis

Partager