24/04/2026
UTHENGA KWA AMENE AKUSAKA NTCHITO
Pakapezeka mwayi ochita nawo maphunziro maka awa "short course" kumapanga nawo zimaonjezera mwayi ku qualification yomwe mulinayo.
Kuti muchite nawo maphunziro wa, mukuyenera kukhala ndizithu izi;
1. Lamnya yotubwanya (smart phone)
2. Ntoro wa internet
3. Mukhale mumatha kuyakhula komaso kumva chingerezi ndi chichewa.
4. MK 10,000 ya registration
Kuti mulembetse nawo, tumizani dzina ku number iyi +265 997 25 68 87