31/08/2026
π BEFORE YOU BUY ONLINE, CHECK THESE 8 THINGS!
Online shopping can save you time and money, koma musamangogula chifukwa chakuti price ndi yabwino. Before you pay, check these 8 things ππ½
1οΈβ£ Reviews & Ratings β
Always check what other customers are saying. Ma reviews ndi ratings zingakuthandizeni kudziwa ngati anthu ena anakhutira ndi productyo kapena ayi.
2οΈβ£ Return Policy π
Check if you can return the product if it arrives ndipo sikuti ndi zomwe munkayembekezera. A good return policy gives you peace of mind.
3οΈβ£ Seller Reputation π€
Osamangoyang'ana product yokhaβyang'anani seller nayenso. Check their page, previous customer feedback and how they deal with customers.
4οΈβ£ Compare Prices π°
Musamagule kwa seller woyamba amene mwamupeza. Fananizani mitengo kuchokera kwa sellers osiyanasiyana. Sometimes the same product can have different prices.
5οΈβ£ Delivery & Shipping π
Before paying, find out delivery cost komanso nthawi yomwe order yanu ifike. Product ingawoneke cheap, koma delivery ikhoza kukwera mtengo.
6οΈβ£ Product Details π¦
Check the size, colour, material, model and features. Musamangodalira picture yokha. Onetsetsani kuti productyo ndi yomwe mukufunadi.
7οΈβ£ Secure Payment π
Be careful with how you send your money. Musamangotumiza ndalama kwa munthu chifukwa chakuti wakuuzani kuti ali ndi product. Verify the seller and use a safe payment method where possible.
8οΈβ£ Discounts & Promotions π·οΈ
Before you pay, check if there is a genuine discount or promotion. Sometimes m***a kupeza better deal just by asking.
π‘ BUYER TIP OF THE DAY
Don't let a cheap price make you forget to do your homework.
Ma Minutes ochepa checking seller ndi product zingakupulumutsireni ndalama, nthawi komanso ma headache ambiri. π
ππ½ Which one of these do people forget to check most when buying online?
1οΈβ£ Reviews
2οΈβ£ Seller
3οΈβ£ Delivery costs
4οΈβ£ Product details
5οΈβ£ Nothing π
Comment with the number ππ½