Narthex Media

Narthex Media Unlocking hidden creativity

We offer: Marketing, Graphic Designing, Branding, Web Development, Event Planning, Photography & Videography, Offset Printing and Content Creation

Ati kuunvera fungo ukulowa mu golo.Koma aganyu cholinga mutidanitse ndima fans a Man U πŸ˜‚
06/09/2026

Ati kuunvera fungo ukulowa mu golo.

Koma aganyu cholinga mutidanitse ndima fans a Man U πŸ˜‚

Full Time Everton 2:2 Man U Kubwenzetsa pa last minute
06/09/2026

Full Time

Everton 2:2 Man U

Kubwenzetsa pa last minute

M'Malawi wina wamangidwa kamba kopezeka ndi mbewa komaso beef pa Airport ku Chicago mu dziko la US America.
06/09/2026

M'Malawi wina wamangidwa kamba kopezeka ndi mbewa komaso beef pa Airport ku Chicago mu dziko la US America.

Verse of the day
06/09/2026

Verse of the day

Wophunzira wa ku Malawi College of Health Sciences wamwalira chifukwa cha mowa.Malingana ndi kalata yomwe yalenbedwa ndi...
06/09/2026

Wophunzira wa ku Malawi College of Health Sciences wamwalira chifukwa cha mowa.

Malingana ndi kalata yomwe yalenbedwa ndi sukuluyi yafotokoza kuti wophunzirayi yemwe dzina lake ndi Eric Mphaya ankaphuzira maphuziro a Diploma in Biomedical Sciences ndipo anali mchaka cha chiwiri.

Izi zadza pamene Mphaya akuti anapapila mowa wambiri ku mwambo wa open air omwe unakozedwa ku Kamuzu University of Health Sciences, Lilongwe Campus. Thupi la Mphaya likaikidwa kwawo ku Thyolo.

06/09/2026

Mwadzuka bwanji kwanuko?
Happy Sunday to you all.

05/09/2026

Good night good people

  Another draw
05/09/2026



Another draw

Bungwe la UN lagwirizana zogwiritsa ntchito map atsopano pamene continent ya Africa ikhale yaikulu kuposa ma continent e...
05/09/2026

Bungwe la UN lagwirizana zogwiritsa ntchito map atsopano pamene continent ya Africa ikhale yaikulu kuposa ma continent ena onse.

Koma ma banker anapanga training. Izizi sizoona koma πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
05/09/2026

Koma ma banker anapanga training. Izizi sizoona koma πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Mount Pleasant, Along Leslie Road, Near Malawi Blood Transfusion Service
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:30 - 16:30
Tuesday 07:30 - 16:30
Wednesday 07:30 - 16:30
Thursday 07:30 - 16:30
Friday 07:30 - 16:30
Saturday 07:30 - 11:45

Telephone

+265993332560

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Narthex Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Narthex Media:

Shortcuts

Share