Limbani Simenti Music

Limbani Simenti Music IAM Limbani Simenti, CEO & Founder of Ndikuoneni Projects, I sing ndikuoneni music& Positive vibes
(1)

19/04/2026

Chameza nzako usamati chakhuta Asernal ikudwala zedi, ndipo ikukwera chitundu choopsya 💔

Ndi m'mene tikuchitira pa Ndirande Word of Faith Temple international
19/04/2026

Ndi m'mene tikuchitira pa Ndirande Word of Faith Temple international

Mzimayi ofatsa komaso wakhalidwe labwino ndithu,it's her birthday today; ameneyu ndi Mlamu wanga Mada Bakali Maloya chid...
18/04/2026

Mzimayi ofatsa komaso wakhalidwe labwino ndithu,it's her birthday today; ameneyu ndi Mlamu wanga Mada Bakali Maloya chidzukulu cha Mkulukutamoyo

When people stay away from me, while I have you by my side pamenepo ndimati,"yessss", chifukwa ndimadziwa kuti chiphwand...
17/04/2026

When people stay away from me, while I have you by my side pamenepo ndimati,"yessss", chifukwa ndimadziwa kuti chiphwandochi ndidya ndekha.



Ndirande siisunga kape Chombo chateraChangu dzaoneni Orion Capsule anapita ku moon uja wafika kale ku Ndirande,Musadzati...
15/04/2026

Ndirande siisunga kape
Chombo chatera
Changu dzaoneni Orion Capsule anapita ku moon uja wafika kale ku Ndirande,
Musadzati sindinanene mawa mukapeza achina James Chalera ataphwasula

Word of Faith Temple international-Ndirande  🔥
12/04/2026

Word of Faith Temple international-Ndirande

🔥

Zomwe achita anthu anaiwa kupita ku mwezi ndikubwera mu space ya 10 days ndi chizindikiro kuti zonse nzotheka; we just n...
11/04/2026

Zomwe achita anthu anaiwa kupita ku mwezi ndikubwera mu space ya 10 days ndi chizindikiro kuti zonse nzotheka; we just need to push the limits ndithu.
As afar as your eyes can see, so you shall be.
Komatu nde chombochi chadatu ngati chinali ku Agrimal.
Posachedwapa tikuyitanani kumwambo okawona chimenechi chikafika pa Ndirande market.
🤣

🤔🤔🤔
07/04/2026

🤔🤔🤔

‎If someone complains; He is right and if you think He is wrong you are right.Bcoz ‎Nobody is wrong and if you think am ...
30/03/2026

‎If someone complains; He is right and if you think He is wrong you are right.Bcoz
‎Nobody is wrong and if you think am right or wrong you are right..

Leroro kwatentha Kwambiri MOTi sim'mene kuliri   muli kuti?
29/03/2026

Leroro kwatentha Kwambiri
MOTi sim'mene kuliri
muli kuti?

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Limbani Simenti Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share