Chandani Ichi?

Chandani Ichi? Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chandani Ichi?, Blantyre.

Bodza lili umu mmmm!!!!
29/12/2025

Bodza lili umu mmmm!!!!

Ndaba nawo chithunzi ichi from Akometsi... Mzimayi uyu osanama ali ndi khama and wayetsetsa kuti a Malawi naye timuoneko...
06/12/2025

Ndaba nawo chithunzi ichi from Akometsi... Mzimayi uyu osanama ali ndi khama and wayetsetsa kuti a Malawi naye timuoneko.Koma mmm guyz ndakhumudwa ndimmene anthu akutukwanila ku page ya Akometsi... kunyoza zija zoti muthu wamayi atha kuganiza zoti basi ndingosiya kuyimba mwina...

PEMPHO LANGA

A Malawi chonde mzimayi uyu tiyeni timukonde ,amene muli ndikuthekera koti achite bwino chonde tiyeni timukumbukile guyz, inu anzathu amene munatchukanu , chonde tamugwilani pankono mzimayi uyu.Mau anu ,ma post anu ali ndimphamvu yoti amalawi asinthe maganizidwe pa Mmayi uyu please guyz... ineyo ndikuona kuti vuto pang'ono ndi achinyamata omwe akum***andizawo ka lush kawo kakupelewera pang'ono..pomwe ndikuziwa kuti mulipo ena m***a kumutuna, komanso kumuonetsa kumtundu wa amalawi ndi mau anu okha chabe...inde ambiri akamuona akuona ngati ndi mdani wa Jetu kapena kuti abwezeletsa A Jetu pansi ... ayi Maganizo amenewo tiwachotse.Ineyo siine wotchuka kapena nditi woziwika koma pempho langa tiyeni tim***andize munjira ina iliyonse coz kuyetsetsa akuyesetsa.

02/12/2025
01/12/2025
01/12/2025
01/12/2025
30/11/2025
29/11/2025

Komatu umu ma baddie anyozeka 😆...akuti ziselekwete

29/11/2025

Abwana awa alindi nkhanza koma mmmhh 🤔😒

29/11/2025
28/11/2025
27/11/2025

Address

Blantyre

Telephone

+265888690509

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chandani Ichi? posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chandani Ichi?:

Share