BOLA Kunthazi

BOLA Kunthazi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from BOLA Kunthazi, Social Media Agency, Blantyre.

09/11/2023
Ovota alangazidwa kudzavota mwa nzeru pa zisankho za mtsogoleri wa bungwe pa Football Association of Malawi FAM
04/11/2023

Ovota alangazidwa kudzavota mwa nzeru pa zisankho za mtsogoleri wa bungwe pa Football Association of Malawi FAM

Mighty Mukuru Wanderers FC MIGHTY MUKURU WANDERERS
04/11/2023

Mighty Mukuru Wanderers FC MIGHTY MUKURU WANDERERS

President wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers FC wapempha ochemelera kuti adzafike mwa unyinji    Sunday limeneli pa Kamu...
01/11/2023

President wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers FC wapempha ochemelera kuti adzafike mwa unyinji Sunday limeneli pa Kamuzu stadium pomwe MIGHTY MUKURU WANDERERS ikadzasewere ndi FCB Nyasa Big Bulletss

Balawala Vingula wakhala munthu oyamba kubwera poyera kulengeza kuti apikisana ndi a Nyamilandu.By Charles Chataza BOLA ...
31/10/2023

Balawala Vingula wakhala munthu oyamba kubwera poyera kulengeza kuti apikisana ndi a Nyamilandu.
By Charles Chataza BOLA Kunthazi

31/10/2023

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

Ofesi ya mulembi wamkulu Ku bungwe la Football Association of Malawi yatulutsa dongosolo ya momwe zinthu zitayendeleBy C...
31/10/2023

Ofesi ya mulembi wamkulu Ku bungwe la Football Association of Malawi yatulutsa dongosolo ya momwe zinthu zitayendele

By Charles Chataza

BOLA Kunthazi

26/10/2023

Pali anthu ochuluka omwe aonetsa chidwi chopikisana ndi mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno la FAM. BOLA Kunthazi ikuuzani zambiri posachedwapa.

26/10/2023

Mphunzitsi watimu ya FCB Nyasa Big bullets Calisto Pasuwa wadandaula ndi mmene akuluakulu oyendetsa mpira ku Malawi amaikira masewero a mipikisano mdziko muno.

Passuwa walankhula izi pakutha pa masewero omwe timu yake inagonjetsa timu ya Kamuzu Barracks 3-2 mu TNN super league lachitatu pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.

Malingana ndi Pasuwa izi zimachititsa kuti adzitha mphamvu mofulumira zomwe sizingapindulire timu ya dziko lino ya Flames.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BOLA Kunthazi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share