26/08/2026
π ZINA zomwe tikuenela Kupanga Kapena Kuziwa ngati nkoyamba Kugula
β DZIWANI IZI
1οΈβ£ Ogulisa galimoto ndi munthu yemwe tingamutenge k*ti ali ngat aliyense yemwe amakhala akugulisa chinthu chake
....Mwachisanzo
OGULISA MATEMBA amatha kukusimikizilani k*ti ndiguleni awawa si owawa musakaike iwe umagula kukafika kunyumba kuphika kudabwa zikuwawa
OGULISA PHONE amatha kuichemelela fon yake iyiyi ndi yabwino gulano or battery lili umu muka charger lero k*ti uzathe ndek*ti week yonse mugwilisa ntchito ...sopano ukangogula umadabwano k*t after 2hrs moto watha
π OGULISA galimoto ndi chimozimozi anthu awawa naye amakhala akugulisa malonda ake so amatha kuwakomesela mulimonse angafunile ka pali vuto koma kusankha osakuuzani inu vuto mwina mumakaliziwa mutagula kale
β¨οΈ CHOYENELA KUCHITA MCHAN
... Inu ngati ogula galimoto mukuenela kugwilisa ntchito maganizo anu posankha kugula Kapena ayi
... Sizimafunika mumumvele OGULISA ayi koma musatile maganizo anu ngati mwakhutisidwa kugula Kapena ayi
1οΈβ£ Mukapita kogula galimoto onesesani k*ti mwapanga check malo onse oyenela komanso muoasidwe mwayi oyesa galimoto ndipo ngat k*thekela kulipo thilani fuel muese kaulendo ndithu muione nokha k*t ikuenda motani because ngat pangakhale mavuto ena imatha kuulula yokha
2οΈβ£ Kogula galimoto ngat simumazisata mumaenela kupita ndi anthu omwe amazisata akak*thandizeni kukuunikilani
π Komabe ngati mwapita ndi ok*thandizani sizik*tanthauza k*ti mumvele chilichonse angakuuzeni muenela kugula chifukwa cha maganizo anu
.... izi ndunena through my experience ambiri agulisidwapo galimoto zoti sizabwino pachifukwa choti amamvela maganizo a anthu ena nde zimatha k*theka ok*thandizani aja kulandila ndalama kwa ogulisa kukukomedwesani mugule mapeto ake amakhala mavuto ndalama zimakhaka zapita mmazi
π―