Lucius w chimombo Abril - Blue sky

Lucius w chimombo Abril - Blue sky Blue sky

Mwayilandira bwanji 888bets Malawi Manoma? Good morning 🔵
19/01/2025

Mwayilandira bwanji 888bets Malawi Manoma? Good morning 🔵

𝟭𝟬𝟬 𝗠𝗶𝗹𝗹𝗶𝗼𝗻 𝗞𝘄𝗮𝗰𝗵𝗮 𝗶𝗻 𝘁𝗵𝗲 𝗯𝗮𝗴!  Mighty Mukuru Wanderers FC's Chief Executive Officer, Panganeni Ndovi has announced kit ...
19/01/2025

𝟭𝟬𝟬 𝗠𝗶𝗹𝗹𝗶𝗼𝗻 𝗞𝘄𝗮𝗰𝗵𝗮 𝗶𝗻 𝘁𝗵𝗲 𝗯𝗮𝗴! Mighty Mukuru Wanderers FC's Chief Executive Officer, Panganeni Ndovi has announced kit sponsorship of 100 Million Kwacha from 888bets Malawi for the 2025 season. The contract signing is currently under way at Golden Peacock Hotel in Blantyre!

14/01/2025

Zasimikidzika kuti Peter Mponda wasankha Fischer Jahman Kondowe, ndipo Jahman wamvomera kugwira ntchito ndi Peter Mponda.Posatira kubwera kwa Mponda ku FCB NYASA BIG BULLETS azibambowa ali ready kufuna kukhaulisa ma team ena mwa nanu.

14/01/2025

Matimu a osewera akale a Silver Strikers yakuno ku mudzi, Power Dynamos komanso Caps United aku Zimbabwe akuyembekezereka kutenga nawo gawo mumpikisano wa masewero ophwetsa mimba omwe matimu a osewera akale a FCB Nyasa Big Bullets ndi Mighty Mukuru Wanderers akhale nawo chaka chino.

Izi ndimalinga ndi Kelvin Moyo, mkulu wa komiti yoyendetsa masewerowa, yemwe wati akukonza kuti phwando la masewerowa likhalepo kumathero a mwezi wa mawa mu nzinda wa Blantyre.

Moyo wati mpikisano wa chaka chino ukhala osinthirapo potengera kuti osewera akale a Silver, Dynamos komanso Caps aonetsa chidwi chodzatenga nawo gawo.

Moyo watinso mphunzitsi wakale watimu ya Bullets, Kalisto Pasuwa, akhala akubwera potengera kuti amatumikira mutimu ya Dynamos.

Ganizo lobweretsa phwando la masewerowa linabwera ngati njira imodzi yofuna kuthandiza omwe anasewerapo matimu a Mapale komanso Manoma omwe pano akuvutika.

Tiyeni tizidekhako
30/12/2024

Tiyeni tizidekhako

30/12/2024
20/10/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Lonex Juwawo, Hope Yaiwa

30/09/2024
28/04/2024

This is my story

Address

Chirimba
Blantyre
MWACHANDE

Telephone

+265883275693

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lucius w chimombo Abril - Blue sky posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Lucius w chimombo Abril - Blue sky:

Share