Francis Yolamu

Francis Yolamu Iโ€™M Francis Yolamu
(Full Stack Developer)
My name is Francis Yolamu C.E.O of malawihostit.com and Ma

26/10/2024

Pano ndik*tha two weeks ndikungopeleka ndekha Good morning and Good night ndizisiyatu ine inzii๐Ÿฅบ

26/10/2024

Ndikufuna anthu 14 amene alibe ndalama k*ti tikwane 15

26/10/2024

Chabwino ifeyo tavomereza k*ti Bullets ndi Team yayikulu team ya fuko kaya amabera kaya samabera koma imatha kumenya mpira๐Ÿ”ฅโœŠ

26/10/2024

Zomapemphana ndalamazo nde ayi aliyense adalandirapo message ya Transporter ndi ya satanic koma munasakha kuyipanga ignore๐Ÿ˜‚

26/10/2024

Ngati Kaliati satuluka ife a Malawi tisiya kumwa ma ARVS ๐Ÿ™„

26/10/2024

Eeh Zosayenda!

Zanga iwe mvela ndikuwuze nkhan yabambo unandipatsa aja, ๐Ÿ˜ญ mmm ndangokhala hule kom chisoni ndili nacho.
Abambo aja tinagwilizana zoti akandipatsa k35 ,000 ndipo napitad takumana mpaka ku lodge.
Titacheza koyamba tinapuma kudikila yachiwili then phone yawo yayitana, Ayiyankha anali akaz awo. amawuza chakudya chathela ana chichele sanadye.
Abambo ajatu pomuyankha mkaz wawoyo amvekele mesa ndakuwuza k*t ukabweleke ndalama nditumiza mwezi ukatha zikalowa pano ndilibiletu. akaziwo at napita kobwerekako at alibe nawoso ndabwelela.

Ati bas ineso ndalama sizinalowe panopa ndilibe kalikonse. ayidula phone at bas tiyen ticheze komaliza tizipita. tacheza titamaliza takasamba ak*tenga 35,000 tinagwilizanayo kundipatsa. lne ndawawuza ndipatsen number yakaz anuwo ndatumizile 20,000 pa ndalama mwandipatsayi agure chakudya ndi ana, amakana kundipasa ndatumiza 20,000 inali phone mwanga ku number yawo k*t awapangile forward akaz awowo ndikuwone ndipo apangad awatumizila. ndawuza yimban phone mwafunse ngat yafika ndalamayi ndili p***a ndimve. Ayimba akaz awowo at ndalandila massage yandalama ndipo ndayamika amuna anga ambuye akupaseni mphamvu apapa ndikufuna thamange ndikatenge pa agent ndigule zakudya ana adye kusanadesese.

Ndawuza zoona uzikalipila chigololo 35,000 kunyumba ana ako ali ndinjala nzeru uli nazo koma. ndanyamuka ndasiya atangogwira mmutu misoz yik*tuluka mmaso mwawo chisoni chinagwira. Akaz awowo ali kuzomba amunawa at kuno abwela kuntchito yokhoza nsewu kulilongwe kuno. bresser okanika kusamala banja lake busy kugula chigololo ana kunyumba ndi mkaz akusowa chakudya.

Ndangokhala hule km umunthu ndili nawo nakhuzika kumvela chisoni mkaz nzanga ndiwana ake

Azibambo tikupusa๐Ÿ™Œ

We are still the best web hosting company! ๐ŸŒ๐ŸŒŸ We've got the perfect web hosting Package for you, tailored to your needs....
24/10/2024

We are still the best web hosting company! ๐ŸŒ๐ŸŒŸ We've got the perfect web hosting Package for you, tailored to your needs. ๐Ÿ’ป๐Ÿš€

With Only MKW4000 You can Secure Your own Cpanel
๐‚๐จ๐ง๐ญ๐š๐œ๐ญ - 0888512159๐Ÿ“ฒ
๐ฐ๐ž๐›๐ฌ๐ข๐ญ๐ž- www.malawihostit.com

24/10/2024

Osamangot work hard bro nafe tipaseni number ya sing'angayo ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

24/10/2024

Good morning and it's throwback Thursday

Primary school yanu munayimbira k*ti kodi?๐Ÿ˜Ž๐Ÿ‘

Aphunzitsi olimbikitsa kupisira aja anali ndani?

One of my favorite pictures with my childhood friend! It represents family, love, brotherhood, loyalty, hard work, consi...
23/10/2024

One of my favorite pictures with my childhood friend!

It represents family, love, brotherhood, loyalty, hard work, consistency, growth, progress, talent, Godโ€™s Grace, Godโ€™s blessings and legacy!

We took this picture about 4 years ago when he visited me Macheke!!.

Tchamani!!โฃ๏ธ๐Ÿ”ฅ

Breaking News  ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™ŒElon is Cureently working on a new version of Robots that can carry your baby for 9 months while you go...
23/10/2024

Breaking News ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ

Elon is Cureently working on a new version of Robots that can carry your baby for 9 months while you go about your work . You and your husband just need to bring your spรจล™ms and eggs . They fertilize and allow it to grow inside the robot for 9 months .

This is going to reduce the number of women that dรญe during Delivery .

Japan constructed a $20 billion Airport in the ocean, but it is now sinking.Japanโ€™s Kansai International Airport, locate...
22/10/2024

Japan constructed a $20 billion Airport in the ocean, but it is now sinking.

Japanโ€™s Kansai International Airport, located on an artificial island in Osaka Bay, Japan, is an impressive feat of engineering that opened in 1994 at a cost of $20 billion. Built to alleviate land constraints, the airport was constructed on soft, alluvial soil, which was expected to settle over time. However, the rate of sinking turned out to be faster than initially predicted. To mitigate the issue, engineers installed thousands of steel pilings to stabilize the ground. Despite these measures, the island continues to subside by several centimeters each year.

Ongoing efforts, including raising runways and adjusting infrastructure, have helped keep the airport functional. However, the high costs and continuous maintenance required pose long-term challenges. Kansai Airport remains an essential hub for international travel, but its future depends on the success of these engineering interventions. The airportโ€™s situation highlights the complexity of building large infrastructure projects in challenging environments.

Address

Balaka
Blantyre
265

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Francis Yolamu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Francis Yolamu:

Share

Category