JIN39

JIN39 Download the best musiq

12/12/2025

M'busa wa nkhosa zosochela anthu ndiye akuchitama ati stuff chikumaitsata bho. Kaya Inu maganizo Anu ndi otani???

Zikuchitikadi  izi!!! Anthu simukulankhula bwino ndiye mwati galimoto ndalama zake ndi misonkho ya a Malawi🇲🇼
21/09/2025

Zikuchitikadi izi!!! Anthu simukulankhula bwino ndiye mwati galimoto ndalama zake ndi misonkho ya a Malawi🇲🇼

Kunena chilungamo northern region ichi anakupangini ichi ndi chipongwe.
20/09/2025

Kunena chilungamo northern region ichi anakupangini ichi ndi chipongwe.

Mwamukumbukira mkulu uyu Balthazar amene anagonana ndi azimai 400 uja court ya mugamula kuti akakhale kundende kwa zaka ...
03/07/2025

Mwamukumbukira mkulu uyu Balthazar amene anagonana ndi azimai 400 uja court ya mugamula kuti akakhale kundende kwa zaka 18 pa milandu ya katangale(corruption).

25/11/2024
25/11/2024
25/11/2024
Kutchena kosaona nyengo the landlord opanda nyumba Gwamba  ulemu wanu
17/11/2024

Kutchena kosaona nyengo the landlord opanda nyumba Gwamba ulemu wanu

13/11/2024

Ma pad a purity omwewa mpaka kumuyimbira mwana wa eni ake ka 40? Purity weniweni yu?😪

Download the best musiq

13/11/2024

*MOZAMBIQUE*

Chipata cha malire a pakati pa Maiko a South Africa ndi Mozambique, chomwe chimatchedwa kuti Libombo, kumbali ya Dziko la South Africa, komanso Ressano Garcia, kumbali ya Dziko la Mozambique chatsekedwa kamba ka zionetsero zokwiya ndi zotsatira za chisankho cha Mtsogoleri wa Dziko la Mozambique.

Chipata chimenechi chotchedwa Lebombo kumbali ya Dziko la South Africa, chili Mchigawo cha Dzikolo, chotchedwa Mpumalanga, pamene chipata cha mbali ya Dziko la Mozambique, chimatchedwa Ressano Garcia, chili Mchigawo cha Maputo.

Padakali pano kumbali ya chipata chimenechi cha mbali ya Mozambique pali Asilikali komanso Apolisi ambiri omwe akuteteza chipata chimenechi pamene zionetsero zikupitiira.

Tikhale tikutsatira komanso kufotokoza zambiri pa Zionetsero zimenezi.

📝NEWS UPDATE

Address

M1
Chikwawa

Telephone

0999216163

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when JIN39 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share