25/01/2024
Like the page for more update 🥺
MWAI KUSIYANA PART 1
Ndnali nd nzanga yemwe tinkakondana kwambiri kuchokera ku primary yathu moti makolo athuso ankaziwa k*ti a2fe timacheza bwino kwambiri
Timalemba mayeso athu a STD8 koma mwamwayi anatisankhira school imodzi moti iyi inali nkhani yabwino kwambiri kwa makolo athu
Inakwana nthaw yot tinyamuke tizipita ku xool yomwe yinasankhiridwa and makolo a2 anatikonzekeretsa bwno nd2
Koma titafika ku xool kuja tinakumanako nd mphunzsi wina yemwe anawauza makolo anga k*t ndzikakhala kwawo coz ndawasangalatsa akufuna azindthandza makamaka kumbali yazinthu zofunika ku xool kuja.koma makolo anzangayu sizinawasangalase chifukwa ankaganiza k*ti tizikhalira limodz.
Mzanga uja anali okhumudwaso kwambiri koma pot amati chokudza mawa sichiimba ng'oma iye sankadzwa k*t k*tsogolo kwake alandla zotan
Wait for another part mumve zomwe anachitiridwa and zomweso nane zinandchitikira