Malawi Wathu

Malawi Wathu ✓News
✓Updates
✓Entertainment
✓Political events coverage
(3)

24/05/2026
24/05/2026

A Njawala ati sizobisanso a MCP alinawo ndi Nkhani🤣🤣

24/05/2026

Anachita bwino kuwathira teargas a Chakwera ndi anthu awo pa tsiku lokumbukila Kamuzu, chifukwa Ali muboma amalekelera anthu akukhapidwa apolisi ndi MDF Ali pompo- Njawala

24/05/2026

Taitana zipani zonse kupatula a MCP kumwambo okumbukila malemu Chilima pa 10 June pano- Felix Njawala

24/05/2026

Mwana uyu waulula momwe zikhalira anyamata a makanja 🤣🤣Taziwa nawo

24/05/2026

Wakhala Moyo ovuta kwambiri popanda a Chilima ku UTM ngakhale tili ndi a Kabambe- Njawala

23/05/2026

Chigoli cha Blue Eagles lero pa civo stadium. Khalangati idalinso offside ambiri akutelo😜

23/05/2026

Tonse ndifedi ojiya ndakhulupilira, timangosiyana ma departments ndi ma sections🤣🤣

23/05/2026

Kholo linalililonse limasangalala mwana wake akalowa mubanja mwadongosolo🤣🤣asiyeni akondwe

23/05/2026

Ndalama sadyela ku Blantyre tiyeni ku Mangochi🤣🤣Akutelo mwini chuma🤣

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Wathu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category