22/08/2026
Ndamaliza kuphika bwela uzajambule iwe....ine pikiti pikiti pikiti basi kufika pamene paja kumpatsa wakaBaza dollar yake kufika kumpanda kukungonunkhila ma spice amwene basi kuzilangiza kuti iyayi panga zomwe wabwelera ife basi khetche....kenako kusinthaso angle basi khetche tikamaliza atigaile kachiboda tizivaya kukapanga edit