Mwachisosa producers and marketing cooperative society

Mwachisosa producers and marketing cooperative society Mwachisosa producers and marketing cooperative society limited is a registered cooperative society u

15/01/2021

COVID 19 IS REAL.
Stay safe

Aliense anabadwa kwa mzimayi.Palibe chifukwa chomachitira nkhaza munthu wamkazi.Tiwateteze amayi ndi ana Ku nkhaza.Mukao...
27/11/2020

Aliense anabadwa kwa mzimayi.
Palibe chifukwa chomachitira nkhaza munthu wamkazi.
Tiwateteze amayi ndi ana Ku nkhaza.
Mukaona wina akuchitira nkhaza amayi kamunenezeni,
Inu ochitidwa nkhaza ululani za nkhazazo.
Wina akakunyozani kamunenezeni.
Uthengawu ukuchokera ku magulu a alimi achizimayi.

27/11/2020

A MALAWI ANZANGA,
Zikumvetsa chisoni tikaona nkhaza zomwe akuchitidwa ana ndi amayi mmakomo.
Ena akuulura ena ayi.
Omwe sakuulura amaopaso kuti akatelo muziwasala ndikuwanyoza.
Tieni tigwilane manja pothetsa nkhaza

14/11/2020

Welcome Donata MacLean

19/09/2020
31/08/2020

Thanks and welcome Maclean David

24/08/2020

thanks and welcome Enock chitseko

proud farmer
23/08/2020

proud farmer

18/08/2020

Kwa amene mumagula masamba a ndiwo ngati: mkhwani,kholowa,thelere la denje ftesh,lobala, mamuna aligone,bonongwe,kholowa wa mdambo,chammwamba ndi khwanya.
Tiuzeni zilipo ndizomwe akulima ma young women kuno.
Ngati njira imodzi Yowalimbikitsa atsikana pa ulimi.
Around lilongwe akupanga deliver.
Tieni tiwagule pofuna kuwatukula mmoyo wawo wa tsiku ndi tsiku

Address

C/o Ching, Ombe Box 73 Lilongwe
Lilongwe

Opening Hours

09:00 - 17:00

Telephone

+265996705168

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mwachisosa producers and marketing cooperative society posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mwachisosa producers and marketing cooperative society:

Share