NAFY AGRO dealers

NAFY AGRO dealers We sell ,seeds, fertilizers,farm equipments, pesticides, herbicides and many more

01/02/2026
we have Xp_16LT sprayers
01/02/2026

we have Xp_16LT sprayers

we have received HD550 20L sprayers 0990398221 call us
01/02/2026

we have received HD550 20L sprayers 0990398221 call us

tengeru select  10g and 25g 0990398221
20/01/2026

tengeru select 10g and 25g 0990398221

12/01/2026

Confidor ndi mankhwala omwe ndi systemic omwe amathandiza chiswe chakumunda kupatula chiswe mankhwalawa amapha a Kodi Kodi( mearly bug) nkhanu anunkhadala chiswe timapopela kamodzi kenako next season, pomwe zinazo mmapola every 7 days for at least twice mulingo wake ndi 6 g in 10 L of water ndipo umathila paphando pa acre pamafunika 8 sachets ngati mufuna minve zambili imbani Ku 0990398221 Nafy agro dealers Kuli mumlimi tili konkoooooooooo

Prize ndi mankhwala omwe ndi direct  contact timapopera kamodzi amapha ntchembele zandonda, kapuchi komanso nsabwe ndipo...
10/01/2026

Prize ndi mankhwala omwe ndi direct contact timapopera kamodzi amapha ntchembele zandonda, kapuchi komanso nsabwe ndipo amapha ndimazira omwe infact stage iliyonse yambozi imafa instant kapena t**i pompo pompo ndipo timapopela motele 10 g of prize mu 16 L of water sprayer ndekuti sachet ya 100g timatulutsa ma sprayer 10 a 16 L for more funsani Ku Nafy agro dealers kuti m***andizike mwachangu watsup us 0990398221

Mvura ikachuluka tomato expand plus Nitrogen akachuluka so  Spray Copper kuti winayo yemwe sanapange izizi akhala bwino ...
08/01/2026

Mvura ikachuluka tomato expand plus Nitrogen akachuluka so Spray Copper kuti winayo yemwe sanapange izizi akhala bwino ndithu ngati pali zofunsa zina m***a kutiimbila phone Ife a Nafy agro dealers pa number iyi or watsup 0990398221 ndipo mudzanvanso zambili

Onse Woteteza komanso kuchiza chiwawu  Manlaxy Active ingredients( Matalaxy and Macozeb)  Contact fungicides Foliar Cure...
08/01/2026

Onse Woteteza komanso kuchiza chiwawu Manlaxy
Active ingredients( Matalaxy and Macozeb) Contact fungicides

Foliar Cure
Active ingredients (Tebuconozole) Systemic fungicides

Cleaner / Bravo
Active ingredients ChlorothanilolManlaxy is more effective then Cleaner last Foliar Cure
NOTE : Foliar Cure works best at early stage in Vegetable crops but works best in Legumes zonsezi muzipeza Ku Nafy agro dealers Kasungu pa boma opposite kulima gold kukhota pa nyika bakery nsewu wa dhumisani ndi Ku lilongwe wakawaka opposite simsol ma numbers anthu ndi 0990398221imbani or watsup mukapezanso ulsngizi waulele

02/01/2026

NPk fertilizer 150 pin and urea 150 pin mchinji kamwendo available

Address

Kasungu
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NAFY AGRO dealers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share