Ghetto ikambe

Ghetto ikambe Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ghetto ikambe, Marketing Agency, Lilongwe.

New Music Alert 🚨 ⏰ on 19th Audio and pa 20 video Sept 2024 🔥
16/09/2024

New Music Alert 🚨 ⏰
on 19th Audio and pa 20 video
Sept 2024 🔥

07/11/2023

Zakhala bwanni Kodi za unisaa?

Ndangova zoti kaya namadingo ndi Mr hide my I'd atani kaya ?

Ayii angofanana 😎Si taye girini
19/10/2023

Ayii angofanana 😎
Si taye girini

AZIBUSA APEMPHA A MALAWI KUTI APEMPHELELE DOROTHY SHONGA ZIWANDA ZAMUCHULUKILAPastor Oliver Phiri ampingo wa Seventh Day...
19/10/2023

AZIBUSA APEMPHA A MALAWI KUTI APEMPHELELE DOROTHY SHONGA ZIWANDA ZAMUCHULUKILA

Pastor Oliver Phiri ampingo wa Seventh Day Adventist SDA ati ngokhumudwa ndizomwe anachita Dorothy Shonga pamodzi ndimamuna wake Zeze pojambula kanema akuchita zachisembwele muchipinda mwawo.

Phiri wati kugonana ndi ntchito za satana zomwe zimakhala zongokondwelesa thupi ndipo a Malawi sakuyenela kumaziyika panthumikila mpaka kufika pomazijambula akuchita mchitidwe wonyasawu.

Phiri watinso zomwe Dorothy Shonga anachita ndizinthu zolawura a Malawi maka ana achipepele mudziko lino ndipo wapempha a Malawi kuti amuyikize mumapemphero satana akumugwilisa ntchito.

"Dorothy Shonga ali ndiziwanda zoophya kwambili zokhulupilira chisembwele, ameneyi akuyenela kuyikizidwa mumapemphero asanafalise ziwanda zoyipazi kwa anthu ena maka m'bado wamuma 2000" anadandaula motelo Phiri akumenyesa bible lake pa chidale.

MANA NEWS ONLINE

19/10/2023

Yabeba ndiyiti Kodi 🤣🤣

Good morning fam

Rest eazy Thomas Chibabe 😭😭😭
18/10/2023

Rest eazy Thomas Chibabe
😭😭😭

Abambo ndaMayii eeet?Demio boy
18/10/2023

Abambo ndaMayii eeet?

Demio boy

Mkazi wa Tay green uja nduyuuu kodi?
18/10/2023

Mkazi wa Tay green uja nduyuuu kodi?

Fana wa ghetto
18/10/2023

Fana wa ghetto

Chidzulo chabho kwama followers anga nose amene mumapanga support artist wanu wa Dancehall 🙏❤️ 🇲🇼
zabwino zinakabwera for now lets keep streaming UDABWA uku tikudikila video yache yapamwamba

https://baobabmusik.lnk.to/UDABWA

Ngakhale amanamizila gheeto komabee big up ntchanaaa
18/10/2023

Ngakhale amanamizila gheeto komabee big up ntchanaaa

A Big Thank you to the Artist 🙏

18/10/2023
18/10/2023

Medaulo 🙌🏾

Check their new video FAST FAST 🔥

BEE JAY & Ace Jizzy

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ghetto ikambe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share