Koche Water Users Association

Koche Water Users Association Koche Water Users Association (KWUA) is a community-based water management organization established in 2012.

Based in T/A Mponda, Mangochi, we are committed to providing sustainable potable water and sanitation services to the community.

Notice: KUKWERA MITENGO YA MADZI - KWUA Ife a KWUA tikweza mitengo ya madzi kuti tipitilize kukonza ndi kupitiliza kuper...
05/08/2026

Notice: KUKWERA MITENGO YA MADZI - KWUA

Ife a KWUA tikweza mitengo ya madzi kuti tipitilize kukonza ndi kupitiliza kupereka ntchito yabwino, popeza madzi ndi moyo. Zimenezi zathandizanso kuti tisamalire ndi kupopera madzi aukhondo mokwanira.

Mitengo iyi ikugwira ntchito pa mabilo a July-August 2026.

1. MITENGO YATSOPANO

· Pakhomo (MK/M3): MK1,110 (kuchokera MK850)
· Malonda (Commercial) (MK/M3): MK1,370 (kuchokera MK1,050)
· Kioski: MK1,500 (kuchokera MK750)
· Meter Fee (pakhomo): MK1,000/mwezi (kuchokera MK500)
· Meter Fee (Commercial): MK1,500/mwezi (kuchokera MK1,000)

2. KUYITANITSA MADZI PA MTUNDA WA 24M (MINIMUM DISTANCE)

· 20mm paipi: MK95,000 (kuchokera MK75,600)
· 25mm paipi: MK99,500 (kuchokera MK80,600)

3. CHINDAPUSA

· Kulumikizanso madzi akadulidwa: MK5,000

KULIPIRA: Imbani *211 # → 3 → 3 → 1 (KWUA). Ikani nambala yanu ya MHMD ngati reference kuti malipiro anu alembedwe bwino.

Zikomo chifukwa chotithandiza kukonza ntchito zathu. Madzi ndi moyo!

20/04/2026

KWUA BILLING CYCLE / NDONDOMEKO YA MA BILLO

KWUA imagwiritsa ntchito njira ya postpaid (mumagwiritsa ntchito madzi kaye, kenako mumalipira).

Momwe zimayendera:
21 February – 20 March
→ Nthawi yogwiritsa ntchito madzi
21 March – 20 April
→ Nthawi yolipira madzi omwe adagwiritsidwa ntchito
Chikumbutso:
Lero, pa 20 April, ndi tsiku lomaliza lolipira bill ya madzi ya nthawi yapitayo.

Tikupempha makasitomala onse kulipira lero kuti apewe kudulidwa kwa madzi.

Please make sure to pay within the payment period to avoid service interruption.

15/04/2026

KWA MAKASITOMALA ONSE: GAWANANI LINK IYI

Tikukupemphani kuti mugawane WhatsApp group yathu ndi:

● Anzanu
● Amnansi anu
● Aliyense amene akufuna kudziwa zambiri za madzi kapena kufunsira kulumikizidwa kwatsopano

Group link:

28/01/2026

Okondedwa makasitomala,

Ma bill a madzi a nthawi ino atuluka. Tikupempha makasitomala kulipira ma bill awo kuti ntchito za KWUA zipitirire bwino.

Zikomo chifukwa cha mgwirizano wanu.

23/01/2026

Dear customers,

KWUA would like to inform you that, due to ongoing operational challenges, the water supply may experience intermittent interruptions. To ensure fair access, water distribution will be rationalised.
More information regarding the rationing schedule will be communicated shortly.

In the meantime, customers are encouraged to collect and store water whenever it is available.

23/01/2026

Water saving reminder

We know water has been unpredictable, and some people leave taps open so they don’t miss it when it starts.

Unfortunately, unattended open taps can waste a lot of water in a short time, affecting supply for others.

Please remember to close taps when leaving and open them only when water is available.

Small actions help us all. Thank you.

Address

Off Mangochi – Monkey Road, Maldeco Trading Centre, Near Koche Primary School Below Nkopola Hill
Mangochi

Opening Hours

Monday 07:30 - 04:30
Tuesday 07:30 - 04:30
Wednesday 07:30 - 04:30
Thursday 07:30 - 04:30
Friday 07:30 - 04:30
Saturday 07:30 - 12:00

Telephone

+265884553575

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Koche Water Users Association posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Koche Water Users Association:

Shortcuts

Share