M'dala chikowa gettoh

M'dala chikowa gettoh Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M'dala chikowa gettoh, Muona, Mangochi.

Bwinotu bwino mungayamwe nazo chizonono cha labala πŸ’”πŸ˜­πŸ˜Ή
26/06/2025

Bwinotu bwino mungayamwe nazo chizonono cha labala πŸ’”πŸ˜­πŸ˜Ή

25/06/2025

Kuyamba dazi pakhomo pamakolo ndi mwano waukulu zedi πŸ’”πŸ€£πŸ™Œ

25/06/2025

Dzulo anati sapita kwawo kwada lero ati akapita azikati anali kuti? 😩😩 kodi Banja amalowa Chonchi πŸ’”πŸ˜­

25/06/2025

Kodi Ndizotheka Msing'anga
Kutha Mphezi ? πŸ’” 😫

Muthu ndiwe tumbuka km matama akewo ngati ankolo ako sazakusithanisa ndi ng'ombe tuπŸ’”πŸ˜Ή
25/06/2025

Muthu ndiwe tumbuka km matama akewo ngati ankolo ako sazakusithanisa ndi ng'ombe tuπŸ’”πŸ˜Ή

24/06/2025

Doctor πŸ‘¨: pepan a patient takupezan ndi sugar
patientπŸ‘΄: ma packet angati?
πŸ’”πŸ™„πŸ€¦β€β™‚οΈ

24/06/2025

Aphuzitsi aja apangisa passport kaya akupita kuti πŸ’”πŸ˜Ή

Born Chriss wabangula mokweza ndimomwe akuyendera mavuyuzi anyimbo yake yasopano πŸ’”πŸ€£πŸ€£
23/06/2025

Born Chriss wabangula mokweza ndimomwe akuyendera mavuyuzi anyimbo yake yasopano πŸ’”πŸ€£πŸ€£

23/06/2025

kukhala Nyumba ya Malata okha okha ku JON kuno sichifukwa kuti muzigogoda Pali ponse ayi Ili ndi chitseko Nyumbayi πŸ˜πŸ’”

23/06/2025

Izi zomati iwe iwezi zithe coz enafe ndife a police titha kumanganapo pano πŸ’”πŸ™„

22/06/2025

Kodi mkazi akamaziluma mulomo wa mmusi mkumakuyang'ana mofooka chimakhala chani? πŸ˜„πŸ™Œ

Address

Muona
Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M'dala chikowa gettoh posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share