Rock Visuals

Rock Visuals Is a production team providing photography, videography, graphical and printing services.

πŸŽ“ *2026 Graduation Season is Here!*πŸŽ‰Kwa onse omaliza maphunziro awo a Form 4 m'masukulu a ku Mulanje β€” nthawi yakwana yo...
22/05/2026

πŸŽ“ *2026 Graduation Season is Here!*πŸŽ‰

Kwa onse omaliza maphunziro awo a Form 4 m'masukulu a ku Mulanje β€” nthawi yakwana yojambula zithunzi zokongola za Graduationyanu!

Rock Visuals ikukupatsani mwayi wosaiwalika wa:
- Professional Graduation Portraits
- Group & Family Photos
- Cap & Gown Sessions
- HD Photos ndi Videos

M'masukulu awa:
- Chinyama CDSS
- Satemwa CDSS
- Dzenje Secondary School
- Seed Of Hope PVT Secondary School
- Salabango CDSS
- Nansomba Secondary School
- Mendulo CDSS
-Chikhwaza Secondary School ndi ena ambiri

Mukufuna kujambulitsa tsiku lanu lapadera? Timabwera ku school yanu nkuzajambula . Booking ikuyamba tsopano

πŸ“ž WhatsApp or Call: 0993555131
πŸ“ Along M2 Road, Chinakanaka Trading Centre, Mulanje

Tag mzanga, mlongo, kapena mwana wanu omwe akumaliza Form 4 m'chaka chino πŸ‘‡
Let’s make your graduation memories legendary! ✨

Birthday iliyonse kuti ikome imafunika mutenge ma pictures oti muzizakumbukila! Happy birthday Jacque 🍰🍾apa tingoti chak...
22/05/2026

Birthday iliyonse kuti ikome imafunika mutenge ma pictures oti muzizakumbukila! Happy birthday Jacque 🍰🍾apa tingoti chaka chasopano ndi picture yatsopano thanks for choosing Rock visuals. Nzomwe timapanga mukakhala ndi birthday ma pictures owala bwino happy birthday to you! Inu birthday yanu iliko liti? Tizipukuta ma camera πŸ“ΈπŸ™‚

HD ndiyochuluka kwambiri koma nanga ili ndi quality yachabe? Timakamba ife pano kuti HD+ ili ku Rock Visuals. Kungojambu...
20/05/2026

HD ndiyochuluka kwambiri koma nanga ili ndi quality yachabe?

Timakamba ife pano kuti HD+ ili ku Rock Visuals. Kungojambulisa chithunzi ku Rocky Gallery uja amakukanani uja mwagwila basi 😁 Ena nkumafunsa kuti "How?" Hahaha ma beb amafila anyamata ofilika kwambiri uja amanyada uja kungomuonesa picture yanu yokhala ndi Chizindikiro cha Rocky Gallery yekha amangomwetulila akatelo amangoti koma ndiye waoneka Bho! Apa imakhala nkhani yayambika πŸ˜πŸ˜€

Ife a Rock Visuals timabwela komwe muli kaya ndima Birthday, Wedding, Music video, HD+ Pictures, kaya ndima Brand logos Zonseso timapanga kuti muziwe zambiri tiimbileni pa number iyi or pa Wap 0993555131 Mitengo yathu ndiyokomera inuyo.
Osaiwala kutipanga like komanso follow,

(Optional )
mukakhala Top fun muzajambulidwa HD Picture yaulele

19/05/2026

Tinadya Mpunga wa Nkhuku ku Chinkhoswe cha anthu awa Vincent ndi Ulemu

Ndi chifukwa chiyani Rock Visuals ndi yabwino kwambiri? 1. Zithunzi za HD quality zenizeni 2. Editing yabwino kwambiri y...
18/05/2026

Ndi chifukwa chiyani Rock Visuals ndi yabwino kwambiri?
1. Zithunzi za HD quality zenizeni
2. Editing yabwino kwambiri yomwe imakupangitsani kuwala
3. Timabwera komwe muli (Mulanje, Thyolo, Zomba, Chiradzulu, Blantyre, Chikwawa, Nsanje, Villa Milange)
4. Mtengo wabwino: K3000 per HD photo

Mukufuna ma pictures a Birthday, Engagement, Family, kapena Music Video?

Inbox or call/WhatsApp 0993555131 tsopano!

Rock Visuals - Where moments become legends πŸ”₯

πŸŽ‰ Zikomo kwambiri kwa makasitomala athu odzipereka! Rock Visuals ikukupatsani chithunzi chokongola kwambiri cha chaka ch...
18/05/2026

πŸŽ‰ Zikomo kwambiri kwa makasitomala athu odzipereka!

Rock Visuals ikukupatsani chithunzi chokongola kwambiri cha chaka chino. Chifukwa cha inu, timatha kujambula ma moments osaiwalika β€” ma Birthday, ma Wedding, ma Music Video, ndi ma Couple Shoots!

Muli ndi chithunzi chabwino kwambiri? Tag Rock Visuals ndipo abwele kuno

Book your next session lero pa 0993555131
Located: Along M2 Road, Chinakanaka Trading Centre, Mulanje

πŸ“Έ Mukufuna zithunzi zina zokongola kwambiri? Ndi nthawi yoti mubwere ku Rock Visuals! Kaya ndinu makasitomala athu akale...
18/05/2026

πŸ“Έ Mukufuna zithunzi zina zokongola kwambiri?

Ndi nthawi yoti mubwere ku Rock Visuals!

Kaya ndinu makasitomala athu akale kapena mukubwera koyamba, timakupangirani zithunzi zomwe zidzakukumbutsani nthawi zonse.

πŸ’‘ Timachita:
β€’ Birthday & Cake Smash
β€’ Couple & Engagement Shoots
β€’ Family Portraits
β€’ Graduation Pictures
β€’ Music Video & Artist Shoots
β€’ Corporate & Event Coverage

Zithunzi zathu ndi HD quality, edited professionally, komanso mtengo wake ndi wabwino kwambiri. Timabwera komwe muli kapena inu kubwera ku studio yathu.

Makasitomala athu akale amajambulisa ma pictures enanso chifukwa cha quality yathu yabwino. Lero ndi nthawi yanu inu!

πŸ“ž WhatsApp or call us: 0993555131
πŸ“ Location: Along M2 Road, Chinakanaka Trading Centre, Mulanje

Book your session lero ndipo tiwone zithunzi zomwe zidzakupangitsani kuwoneka ngati star! ✨

Tag munthu amene akufunika zithunzi zabwino apa πŸ‘‡

HAPPY BIRTHDAY to our amazing young Client, CollinsπŸŽ‰! πŸ“ΈWant to make your birthday unforgettable? Book a photoshoot at Ro...
30/04/2026

HAPPY BIRTHDAY to our amazing young Client, CollinsπŸŽ‰! πŸ“Έ
Want to make your birthday unforgettable? Book a photoshoot at Rock Visuals Studio and let's create some epic memories 😊!
πŸ‘‰ Call us 0993555131

Address

Mulanje M2
Mulanje

Opening Hours

Monday 07:00 - 18:00
Tuesday 07:00 - 18:00
Wednesday 07:00 - 18:00
Thursday 07:00 - 18:00
Friday 07:00 - 18:00
Saturday 07:00 - 18:00
Sunday 07:00 - 18:00

Telephone

+265885876863

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Rock Visuals posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category