03/08/2026
MUNTHU OWONONGA
Bambo Peter Tholo, azaka 28, amawanga ku Kasungu Municipality atawagwira ndi ma meter a Central Region Waterboard ankhaninkhani omwe Iwo avomela kuti akhala akumaba manyumba mu Municipality yi
A Tholo auza a police kuti ma meter amawasungula ndikupangila zitsulo zina ngati makasu or amakagulitsa kwa ma china ku Lilongwe.
Izizi zinachitika Saturday.
A police atengera a Tholo ku court lerolo