Kung'alula

Kung'alula 14k followers 1.4k following






Kuziwa zochitika pa malawi

Wapha sister wake ndiye anthu okwiya amuchita zinthu mokuti iyeso za moyo kulibe"Makosana Kuno kwa Kachere kwachitika zo...
07/02/2026

Wapha sister wake ndiye anthu okwiya amuchita zinthu mokuti iyeso za moyo kulibe

"Makosana Kuno kwa Kachere kwachitika zoopsa,
Mtsikana wa zaka 16 waphedwa ndi m'chimwene wake uyu pomubaya, koma anthu okwiya anamugwiranso mnyamatayo mpaka naye amuphanso"

Akuti Chifukwa chomwe mnyamatayo wamuphera sister wakeyo taponya mu comment boxπŸ‘‡

07/02/2026

Abwana aku cross roads.

Amalawi mpaka mwafika apa????

28/01/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Sta Breez, Sheck Chakusowezga, Kingsh Remondi Kadesh, Mawini Kanjuzi, Beatman Mailosi, Nephtali Nguluwe, Alice Sibo Kanyinji, Crescencia Teputepu, Sakinah Mwale, Yohane Wodziwika Chisoni, Iness Bonongwe, Peter Duwa, Mabvunika Sarah Manzi, Douglas Γ‡hindaya Machekula, Yasin Mtamira, Rash Ndeule Naduwe, Chicco Marciano, Annie Cv Kasunda, Dorothy Nayuma, Precious Mw, Roadwell Mavuto, Paul Cikopa, Christina Nyamlowoka Chirwa, Rafiki Malifado Mustafa, Emily Pensulo, Maria Msuku, Pilirani Shatta Chimkango, Mphatso Mphete, Rachel Kasupe, Angelique Chiputura, Diana Chanache, Lydia Nchessie, Versace Kungs, Humphrey Obhebha Shasha, G Man Soko, Dorothy Mtambo, Chikondi Phiri, Eunice Louis, Mphatso Watson, Joseph J Banda, Brave Mithi, Prince Kay, England Inusu, Bello Thom, Lucas Paulino Maq, Lottie Nyirenda, Phillips Watsopano Kalima, Memori Chikanga, Puma Mw Prem, Charles Chiwala

28/01/2026

MUITANO.
Ngat munthu anakuchokeran. Kaya amunanu anakuthawan ndye mulbe chovala chake gwilitsan tchto dzina lake ndpo pezan izi.
*mizu ya chanzi mudule timapiece 4
*mizu ya mpepu mapiece 4,
*lipepedwa muchotsa timitengo 4
*mupeza muzu wa chipembere.

KAPANGIDWE KAKE.
*pezan miyala itatu iken mmene timaikira mafuwa aja, tengan mizu yonse ndatchulai ndkuimanga pamodzi ikan pakat pa miyala ija tengan zinyalala pang'ono ndkuika pomwepo ndpo yatsan moto. Ndpo tengan muzu wa chipembere uja ndkuyamb kupanga izi...kulemba ndzovuta pangofunka kuyakhula bas.

Zambiri uku follow 'alula uku nde mukhala anthu odalilidwa mmudzi

25/01/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Tiyamike Banda, Stelia Vasco, Clenkie Constance, Juvie Dem Dem, John Lapson Msambakaluma, Esther Maonde, Monica Mtonga, Maliyane Mtukulah, Ibula Bukhe, Moreen Balala, Cecilia Chikuse, Vincent Lemitala Bikoko, Ring Leader Mw, Chimzy DaDa, Michael Eid

UYU ndi lifalii amene anayimbira masewera a mpira wa miyendo ku Ntchisi lero.Akuti iyeyu anapeleka penalty nthawi yoonje...
04/01/2026

UYU ndi lifalii amene anayimbira masewera a mpira wa miyendo ku Ntchisi lero.

Akuti iyeyu anapeleka penalty nthawi yoonjezera kwa timu ina matimu ali zero kwa zero

Anthu aku Ntchisi ayi ndithu πŸ˜³πŸ™†βš½πŸ†

13/12/2025

MASO AWARDS 2025 BEST EVENT PHOTOGRAPHER MALE AMUNA ACHISALE πŸ“Έ

12/12/2025

Apa pali nkhani

Happy Birthday to Model XaniaπŸŽ‚πŸŽ‰πŸŽŠ
10/12/2025

Happy Birthday to Model XaniaπŸŽ‚πŸŽ‰πŸŽŠ

kwachema anthu awa eeeee check in first comment nkhani yose πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…
10/12/2025

kwachema anthu awa eeeee check in first comment nkhani yose πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…

Address

Blantyre, Chigumula
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kung'alula posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share