22/11/2025
Malinga ndi apule aku Zambia, munthu osauka komanso ochepekera maphunziro ndiyomwe amakhala bize ndikavalidwe. Koma olemelayo kapena ophunzirayo amakhala bize ndi pulogilamu kapena assignment alinayo. Inu muli mbali ityiyo apapa?
Tiyeni Tizingokhala Basi Life Is Options.