25/04/2026
COLLEGE YOPITA OLO OSAPHUNZIRA IJA IYI
Usiku ndachezera kulemba mayina a ophunzira omwe akufuna kubwera ku Mbandira Technical College - Ku Nkhotakota, Mpamantha.
Kutsegulira ndi lolemba lomweli, 27th April 2026.
Koma simunachedwe, chifukwa matsiku obwera ophunzira adakalipobe mpaka pa 9 May 2026.
Koma dziwani izi:
Fees:
K100 000 pamiyezi yonse 5 yophunzira, m***a kupereka half, (K50 000). Inayo kuzamaliza mwanayo ali kale ku school komkuno.
Registration fee:
• K5000, umapereka kamodzi.
Student council fee:
• K5000, umapereka kamodzi.
Hostel fee:
• K10 000, pamwezi.
Mwachidule, ndalama yonse yofunika podzayamba ndi K120 000 yokha basi*.
Koma m***a kubwera ndi:
1. Registration (K5000)
2. Hotel fee (K10 000)
3. Student council (K5000)
4. Half ya School fees (K50 000)
Pamodzi K70 000, ndipo mudzayamba popanda vuto lililonse.
Chakudya mumabwera nacho, mumadya zanu zophika nokha. Mutenge ziwiya.
Kuti mulembetse, ndipedzeni ku inbox ndi information iyi:
1. Dzina la ophunzira
2. Phone number yake
3. Phone number yamakolo
4. Course yomwe mukufuna
5. District
Tikutenga aliyense ngakhale oti sukulu adalekeza Standard 1.
Ma course ndi awa oti musankhe:
1. Tailoring and Fashion Designing (zosoka)
2. Welding and fabrication (Zootchelera)
3. Electrical Installation (Zopanga wiring)
4. Plumbing (zamadzi)
5. Bricklaying (Zomanga)
6. Information and communication Technology (Zama computer)
7. Carpentry (Zokhoma)
Mukamalidza ma course awa miyezi 5 yonse mumalandira certificate kuchokera ku College yathu.
Koma pali ma course awa amafuna wa MSCE, ndipo fees ndi K150 000 pa semester. Ma course ake ndi awa:
● Accounting (ICAM)
● Business Management (ABMA)
● Human Resource Management (ABM)
● Community Development (ABMA)
● Global Food Security & Nutrition (ABMA)
-Ma course awa tikuphunzitsanso online, zikutheka ndithu.
Whatsapp: 0998 124 881
Facebook:
Tikos Che Ndindi (100 000 followers)
Tiktok:
Tikos Che Ndindi (92 000 followers)
Email: [email protected]
Kapena lowani whatsapp group yathu (group 2), chifukwa group 1 yadzadza. Link https://chat.whatsapp.com/EDv5WPBgAb0Ag3glQIOgE8?mode=gi_t