Blankslate LENZ

Blankslate LENZ Content Creator | Digital Marketer
(8)

We at Blankslate Lenz ,we treasure our clients more than anything as we know that the happiness of our clients is our sole mandate.

05/10/2026

Anthu ena achedwa ku ntchito, ena abwerera, kutsata ku cheaper

Anthu Okonda ULEMU Coaches,Dzioneleni nokha m'mene asanjira ndondomeko Yao....
05/10/2026

Anthu Okonda ULEMU Coaches,
Dzioneleni nokha m'mene asanjira ndondomeko Yao....

Amang'alulidwa birthday yake ili pafupi...Hope chaka ichi asinthadi mu Zochitika...Malangizo Ndiye walandira kale...Imag...
05/10/2026

Amang'alulidwa birthday yake ili pafupi...
Hope chaka ichi asinthadi mu Zochitika...
Malangizo Ndiye walandira kale...
Imagine week yonse Kukhalira kumulangiza or atakhala osamva,
Apa pokha amva basi...

Kapena mukufuna kuonjezera malangizo Ena Abale Inu...

Happy Birthday Namwali....
Malangizo aja kuwagwiritsa ntchito chonde..

ZACHISONITaluza mmalawi nzathu kuno ku Theba yemwe dzina lake ndi Yankho Paul Ndipo ku Malawi amachokera ku Mpemba Chakw...
04/10/2026

ZACHISONI

Taluza mmalawi nzathu kuno ku Theba yemwe dzina lake ndi Yankho Paul Ndipo ku Malawi amachokera ku Mpemba Chakwa Chadzunda,, m'mudzi mwa Mwangata Blantyre , pafupi ndi chipatala cha St. Vincent

Iyeyu watisiya m'mawa wa loweruka pa 3 October 2026 m'dziko la South Africa komwe amakhala ndi banja lake

Mzimai yu adali oyembekezera. Koma tsoka ilo watisiya nthawi yobereka , ndipo mwanayonso wapitilira.

Zopweteka zedi, kuluza achibale m'nyengo Ngati Iyi, komanso ku Dziko la kutali...

Mzimu wake ukause mu Mtendere..

04/10/2026

I want to give a huge shout-out to my top Stars senders. Thank you for all the support!

Tuweni Nkhota

04/10/2026

Amai awa amavinatu Asaaa

04/10/2026
04/10/2026

Ulibe ndalama,
Ulibe True Love Komanso Ulibe Agogo Omwe Amatama, Ndiye uli ndi chani pa dziko pano????
Tiyankheni timve, Kuti muli ndani??

ATTENTION ATTENTION ATTENTIONTawerengani izi abale inu...AMBUYE ATETEZENI ANAWA KOMWE ALIKO Ana awiri aku malawi asowa k...
04/10/2026

ATTENTION ATTENTION ATTENTION

Tawerengani izi abale inu...

AMBUYE ATETEZENI ANAWA KOMWE ALIKO

Ana awiri aku malawi asowa ku Cape Town

Masana ano kwatipeza nkhani yomwe yachitika ku Dunoon , Ana awiri,.Alexander ndi Christopher asowa zulo ,Alexander ali ndi zaka 11 ndipo ndipo Christopher ali ndi zaka 12 asowa pamene makolo awo anali atachoka ku ntchito ndipo anafika panyumba anawo amasewera panja ,mwachizolowezi ndiye makolo Poona kuli ziii ana sakubwera zinawapatsa mantha momwe amayang’ana panja ana panalibe around 6pm

amene angadziwe komwe anawa Ali chonde aziwitseni bambo awo pa number iyi

0605003729 Christopher kapangama
Man chester 45 street Dunoon Capetown

04/10/2026

Moyo wapa theba...

Address

227 Mainroad
Cape Town
7800

Opening Hours

Monday 07:00 - 19:00
Tuesday 09:00 - 19:00
Wednesday 09:00 - 19:00
Thursday 09:00 - 19:00
Friday 09:00 - 19:00
Saturday 09:00 - 19:00
Sunday 09:00 - 19:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Blankslate LENZ posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Blankslate LENZ:

Shortcuts

Featured

Share