Innoma-Journalist

Innoma-Journalist Arts & Entertainment | Sports | Gossips | Politics | Developments | PR & Marketing | Research | Media Consultancy
(3)

Canada akuichapa uku, anyamata aku Ghana akuchita kukuwa mpuntheni, mesa watinyozela player wathu ameneyo.34' Canada 0-1...
12/06/2026

Canada akuichapa uku, anyamata aku Ghana akuchita kukuwa mpuntheni, mesa watinyozela player wathu ameneyo.

34' Canada 0-1 Bosnia and Herzegovina

#

Akuti uyu asalowe m'dziko lathu uyu ngwachigololo uyu.Dziko la Canada lakana kuti osewera mpira pakati pa timu ya dziko ...
12/06/2026

Akuti uyu asalowe m'dziko lathu uyu ngwachigololo uyu.

Dziko la Canada lakana kuti osewera mpira pakati pa timu ya dziko la Ghana Thomas Partey asalowe m'dzikolo ponena kuti akuyankha milandu yogwililira.

Partey yemwe akukalowanso mu bwalo la milandu mu mwezi wa November, akuyankha milandu yomwe azimayi anayi anakamusumila ku bwalo la milandu kuti anawagwililira nkuwapanga nkhanza.

Kufika tsiku la lero, Partey sanampeze olakwa ndipo milandu yonseyo anaikana.

"Takonzeka kukumana ndi Bullets, tikudziwa kuti ndi timu yaikulu ndipo timaipatsa ulemu komabe nafe tiikapo mtima kuti t...
12/06/2026

"Takonzeka kukumana ndi Bullets, tikudziwa kuti ndi timu yaikulu ndipo timaipatsa ulemu komabe nafe tiikapo mtima kuti tiwine."

Enos Chatama-Ekhaya Head Coach

 : National Bank of Malawi limodzi ndi Press Trust asaina mgwirizano wa ndalama zokwana K1.2 biliyoni zomangira hostel y...
12/06/2026

: National Bank of Malawi limodzi ndi Press Trust asaina mgwirizano wa ndalama zokwana K1.2 biliyoni zomangira hostel ya ophunzira yolowa mabedi 112, nyumba ziwiri za aphunzitsi komanso chitsime cha madzi ku Njerenje Community Day Secondary School (CDSS) m’boma la Balaka.

Malinga ndi mgwirizanowu, National Bank ipereka K800 miliyoni, Press Trust ipereka K400 miliyoni, pomwe boma kudzera mu Unduna wa Maphunziro lipereka K20 miliyoni.

 : President Prof. Arthur Peter Mutharika and First Lady Prof. Gertrude Mutharika on Friday departed for South Africa on...
12/06/2026

: President Prof. Arthur Peter Mutharika and First Lady Prof. Gertrude Mutharika on Friday departed for South Africa on a private visit. The President left through Kamuzu International Airport in Lilongwe.

Speaking before departure, Mutharika said the trip would be brief and assured Malawians that everything remained under control. He expressed confidence in the country's stability and said he would return within a few days.

12/06/2026

: Minister of Industrialization, Business, Trade and Tourism Simon Itaye has described the K88.8 billion (US$52.8 million) Mariot Ryalls Hotel project as a strategic investment capable of accelerating economic growth, tourism development and employment creation.

Itaye made the remarks on Thursday after touring the hotel construction site at Lilongwe Golf Club, where he appreciated progress on the development being undertaken by Blantyre Hotels plc on 3.271 hectares of land.

Chief Executive Officer of Eris Properties MW, the construction management company, Washington Chimuzu said the investment will generate direct and indirect employment opportunities while stimulating growth among local businesses supplying goods and services to the facility.

Happy Birthday, Charles Mafaiti!
11/06/2026

Happy Birthday, Charles Mafaiti!

Masters FC
11/06/2026

Masters FC

🔴 BREAKING: Islamic Revolutionary Guard Corps (IRGC) ya dziko la Irana yati inagwiritsa ntchito ma bomba (Ballistic miss...
11/06/2026

🔴 BREAKING: Islamic Revolutionary Guard Corps (IRGC) ya dziko la Irana yati inagwiritsa ntchito ma bomba (Ballistic missiles) 12 kulunjika ku katundu wa dziko la USA ku Jordan Al-Azrag komwe kuli zida za nkhondo, komwenso kuli ndege za F-15 komanso F-16 zomenyela nkhondo.

Naye President wa dziko la USA Donald Trump wati, Iran ikupanga chibwana, ndipo ilipira ndalama zochuluka pa zomwe ikupanga. Trump watinso dziko la USA ndi lokonzeka kukambilana ndi dziko la Iran kuti nkhondo ithe.

Koma sikuti dziko la USA langokhalapo chete, nalonso likuvunga mizinga mwa nyo yomwe ikumalunjika chaku mwela kwa dziko la Iran.

Malingana ndi wailesi youlusa mawu ya boma la Iran, Strait of Hormuz yatsekedwa ndipo Iran yachenjeza kuti pasapezeke si...
11/06/2026

Malingana ndi wailesi youlusa mawu ya boma la Iran, Strait of Hormuz yatsekedwa ndipo Iran yachenjeza kuti pasapezeke sitima ili yonse yodutsa.

Masiku awiri apitawa, maiko a Iran ndi America akhala akuthilana machaka kusatira kulepheleja kwa mgwirizano omwe awiriwa akhala akukambilana.

Address

Noll Avenue No 58
Lilongwe
7760

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Innoma-Journalist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share