Moto Salumpha

Moto Salumpha Nkhani Zochita ndi Amalawi komanso m'madera wena Ozungulira. Entertainment | Politics | Business | History I

NKHANI ZA ZIZIZI - Phungu wa nyumba ya malamulo ku ntcheu yemwenso ndi wachiwiri Kwa nduna yoona zachitetezo Hon Norman ...
06/10/2026

NKHANI ZA ZIZIZI -

Phungu wa nyumba ya malamulo ku ntcheu yemwenso ndi wachiwiri Kwa nduna yoona zachitetezo Hon Norman chisale apeleka madeski 180, makope 100,000 ndi makatoni asopo ku masukulu adera lao.

Malingana ndi achisale ati apanga izi pofuna kutukula Dera lao pankhani ya maphunziro monga mmene akufufunira nsogoleri wadziko lino prof peter mutharika.

Moto Salumpha

28/09/2026

School vs reality ( Sukulu vs Tchutchu wa Moyo )

Share ena aphunzileko
Moto Salumpha

Mnyamata wazaka 14, Imran James, ndipo anali mu Standard 8 pa Saint Louis Primary ku Monkey wazimangilira mu nyumba yosa...
28/09/2026

Mnyamata wazaka 14, Imran James, ndipo anali mu Standard 8 pa Saint Louis Primary ku Monkey wazimangilira mu nyumba yosatha kamba kokhumudwa kuti mayi ake anamukakamiza kuti agwire ntchito yomwe iyeyo amakana kuti akuyenela kupanga ndi mtsikana (sister wake).

Mai ake a Imran, Mai Febe Nampunga, anamutuma mwana wawoyi kuti akatumge madzi. Amakana koma anamukakamiza ndiye anangopitabdbmomo. Anabweletsa madziwo kenaka kusowa osawonekanso.

Mai ake ndi abale ena kumufufuza basi kukamupeza akulendewela kudenga wazikwedzeka.

"Iwe Imran basi bwera madzi ndituma sister wako." Akulira Mai ake

Follow Moto Salumpha

28/09/2026

Mbabva

🌿Kodi simukhulupililabe Kuti cinnamon ngoopswa? 🌿Sinamoni amagwila ntchito zambili ndipo 🌿chibwana alibe🌿Kodi  mukufuna ...
27/09/2026

🌿Kodi simukhulupililabe Kuti cinnamon ngoopswa? 🌿Sinamoni amagwila ntchito zambili ndipo 🌿chibwana alibe

🌿Kodi mukufuna ntchito
🌿 Kapena Mukupita kukasaina contract
🌿 Mukupita kuma interview
🌿 Mukupita kukalemba mayeso
🌿 Pa nkhani za maubwenzi
🌿Kapena gambling ndi betting.

🌿 Tengani Vaseline pang’ono ndi cinnamon 🌿pang’ono. Sakanizani bwino pamene mukunena 🌿zomwe mukufuna kuti zichitike.

🌿 Kenako pakani thupi lanu, ndipo mukamaliza pitani komwe mukulowerako

🌿ndipo inuyo zotsatira zake mudabwitsika nazo

🌿 Zinthu zachilengedwe ndizamphamvu ngati 🌿mumakhulupirira .
🌿pangani zimenezo muone Kuti Zinthu Zanu 🌿zisintha motani.

Follow Moto Salumpha

Napoleon Dzombe  | Shepherd bushiri ndi ena achuma Ali ndi ma Degree ??Mwina mwaziyankha nokha chifukwa chimene ambiri t...
25/09/2026

Napoleon Dzombe | Shepherd bushiri ndi ena achuma Ali ndi ma Degree ??

Mwina mwaziyankha nokha chifukwa chimene ambiri tili amphawi ...

Moto Salumpha

25/09/2026

Kuli mafunso kunjaku pakafukufuku wa ndege , inuyo mafunso anu ndiotani amene simukuwamvesa ?

24/09/2026

Mkulu wa kampani ya TNM, a Michel Hebert, ndi adindo ena aku kampaniyi a Peter Munthali ndi Lloyd Gowera, tsopano akuonekera pamaso pa Komiti ya Nyumba ya Malamulo yomwe ikufufuza za ngozi ya ndege ya ku Chikangawa.

Izi ndi mboni zachiwiri zomwe zikuonekera pamaso pa komitiyi lero, a Daudi Suleman omwe anali mkulu wa MACRA atamaliza kupelekera umboni wawo.

(by Sarah Tembo-Lilongwe:09/24/26)

24/09/2026

Bro , chibwenzi chako si sister wako kapena Mai ako .

Let that sink in

Address

Marble Towers
Johannesburg

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Moto Salumpha posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share