Anyakwawa

Anyakwawa Currently what is happening around the world (kudziwisana)

For any business and promotions
+265(0)885516342
+27633681981

Kuyankhula uku sikwabwino chonde
06/09/2026

Kuyankhula uku sikwabwino chonde

British-Nigerian Influencer Wamwalira Atachitidwa Operation Yokulitsa Chida Chake Chowinjira .—Businessman komanso influ...
06/09/2026

British-Nigerian Influencer Wamwalira Atachitidwa Operation Yokulitsa Chida Chake Chowinjira .

—Businessman komanso influencer wa ku Britain-Nigeria, Igho “Tiny” Ubiribo, amenenso anali childhood friend wa oyimba “Davido” wamwalira ali ndi zaka 43 atachitidwa operation yokulitsa chiwalo chachimuna ku Bangkok, Thailand.

Malinga ndi malipoti, atangomaliza njirayi anayamba kumva kupweteka kwambiri pachifuwa ndipo anagwa. Anamutengera kuchipatala china komwe anapezeka ndi pulmonary embolism, yomwe imalepheletsa magazi kuyenda bwino kupita m’mapapo.

Madokotala anayesetsa kuti amupulumutse koma sizinayende.
Mzimu wake upumule m’mtendere 🕊️

05/09/2026

Half-Time⚽
FCB Nyasa Big Bullets 3-0 Silver Strikers
Kwachema

04/09/2026

Kodi ma ARV sangapangeko odzola? okumwawa iii nkhwikoyi yatopa guys 😭😭😭

04/09/2026

Koma guys ndalama ingachepe maka koma ukagwetsa mtima umapweteka, ndataya k200 dzulo koma eeeee sinagone😅😅😅😅

Wathuyi tu bola dressing iyi it's making sense
03/09/2026

Wathuyi tu bola dressing iyi it's making sense

Akuti Mg1 analusa mpaka kumuluma nkazi nzakeyu🤓
03/09/2026

Akuti Mg1 analusa mpaka kumuluma nkazi nzakeyu🤓

Akuti akugonabe since monday😂
03/09/2026

Akuti akugonabe since monday😂

Pachibale pao pheee 😂😂😂
02/09/2026

Pachibale pao pheee 😂😂😂

Koma Jude zoona🤣 Apolisi ku Lilongwe amanga a Judith Phiri azaka 25 kamba kowaganizira kuti akhala akutenga katundu osiy...
02/09/2026

Koma Jude zoona🤣


Apolisi ku Lilongwe amanga a Judith Phiri azaka 25 kamba kowaganizira kuti akhala akutenga katundu osiyanasiyana wa ndalama zokwana K363,000 kwa wamalonda wina mwachinyengo.

Malingana ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Lilongwe, a Khumbo Sanyiwa akuti mayiyu wakhala akutumiza umboni wapafoni wachinyengowu osonyeza kulipira kwa katundu kudzera ku bank (screenshot).

Mwachitsanzo, iwo ati mayiyu pa 19 August anafunsa ogulitsa malonda mu tawuni ya Lilongwe kuti amutumizire katundu wa K88,000 atamutumizira umboni olipira kudzera ku bank wabodza

Source ; Zodiak

Kenaka akuti oganizilidwayu adachitanso izi pa 22 August pomwe anawuzanso ochita malonda uja kuti atumize katundu wa K200,000, komanso pa 26 August pomwe anamuuza wamalondayu kuti atumize katundu wa K75,000.

Koma akuti tsiku la 40 lidakwana pa 31 August pomwe anauzanso ochita malondayu kuti atumize katundu wa K130,000 ndipo anatumizanso umboni wachinyengo osonyeza kuti walipira K150,000.

Address

196 Harrower Road
Port Elizabeth

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anyakwawa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Anyakwawa:

Shortcuts

Share